Anthu anga akuonongeka chifukwa cha kusadziwa. Abale anga mwa Ambuye kukamva mawu muzikhala ngati ophunzira aku beleya omwe amati akalalikidwa ndi paulo amapita kukawerenganso malemba kuti zomwe amaphunzitsa zija ndi zoona? Read your bible then come back to me, bible mulibe mawu oti chauta pa ma verse omwe amawerengawo komanso si buku la malamulo koma chilamulo ndi zosiyana nde osamangothamangira kunena amen mukunamizidwa you have to be very careful bible is a word of God not a magazine.