Тёмный
No video :(

Kachikenaso Born Kalindo 😂🙌😂😂🙌 pa Chi Sunday 14 July 2024 

Malawian Cameras
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 26 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 85   
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Ndalama zingowonongedwa anthu angofa mdzipatalamu mankhwala kulibe anthu angofa sisawawa Mulungu akuwoneni mwapaderadera
@user-nz7bd7lm4i
@user-nz7bd7lm4i Месяц назад
Born mulungu azikudalitsa kwambiliiiiiiiiiiii ndipo azikuteteza🙏🙏🙏
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim Месяц назад
Chakwera akuwalipira azungu pa ntchito yomwe adagwila pakupha chilima
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb Месяц назад
Achakwera akuwononga dziko lathu kwambiri.
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Месяц назад
Dziko lochitisa manyanzi, nkumati achakwera akugwira ntchito ngati president.
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f Месяц назад
Tiyamike kubwera kwa tonse Alliance anthu mukung'alula kuti anthu tiziwe zenizeni more 🔥 🔥
@fredsemu7136
@fredsemu7136 Месяц назад
KOMA CHIKANGAWA ATIPWETEKA NDITHU
@ThokozaniMunkhondia
@ThokozaniMunkhondia Месяц назад
A born kalindo,inu ndi mbambande😢😢
@cjaymw496
@cjaymw496 Месяц назад
Ya balance I think so too😂😂😂
@officemoyenda-rj2hz
@officemoyenda-rj2hz Месяц назад
Koma this very very shameful 😢😢😢😢😢
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 Месяц назад
Koma bon mulungu akuteteze
@ClearKondowe-m3j
@ClearKondowe-m3j 29 дней назад
Very sorry a Malawi kaya dziko lathu likonzedwa. Yoooo
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i Месяц назад
Ati akukonza zinthu!....😅😅😅😅😅😅😅...koma kukonza kunasintha..
@MisheckAselo
@MisheckAselo Месяц назад
Chakwera mchifukwa chake anakapemphera ku CCAP kamutu kataya mission yapheduka, umkaona ngati wapha chilima zako ziziyenda, chilima sanafe akanalipo muona zakuda inu😂
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Месяц назад
Mulungu wakiya nawe chakwera waona mulungu wakwiya ndpo mulungu achita nawe iweyo
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f Месяц назад
Ima poyela ndipo aliyense azimva ndithu.Tinasankha satana
@wonganichakakanyirenda3299
@wonganichakakanyirenda3299 Месяц назад
Chakwera iweyooo
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Месяц назад
KKKKKKKKKK BALANCE KUWAMALIZIRA PANTCHITO YOMWE ANAGWIRA PAKUPHA CHIRIMA NDI ANZAKE SHAME CHAKWERA
@stevenbanda6665
@stevenbanda6665 Месяц назад
Tiuzeni zambiri bwana .kma dziko lathu lomwe kuzunzika
@SumanJames
@SumanJames Месяц назад
Akalindo sakunama
@ZettaImuranYunusu
@ZettaImuranYunusu Месяц назад
Osati Ifeyo Amalawi ai.... But all opposition party's we are with you Trap
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Месяц назад
Munyengo yakung'alula
@crosbeygondwe5403
@crosbeygondwe5403 Месяц назад
Kung'alulaaaa😂😂😂😂
@robertkamtimaleka4394
@robertkamtimaleka4394 Месяц назад
a Born Kalindo 42 million yommweyi basi
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e Месяц назад
Auze DC ❤ agaru amenewo
@AufiThera
@AufiThera Месяц назад
Wathu wathu born kalindo ✌️🔥 Kung,alula💯💪
@user-oy6dl1pv9e
@user-oy6dl1pv9e Месяц назад
The DiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiCiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
@JamesTeacher-b3o
@JamesTeacher-b3o Месяц назад
Bwana inuyo mmatha kuyankhula ulemu wanu
@user-xx4mt8ox8e
@user-xx4mt8ox8e Месяц назад
Mwati ndi Balance?
@Mikekajawo-pq9nr
@Mikekajawo-pq9nr Месяц назад
At we are building Malawi yet ndalama zikutuluka
@DineoKotjomela
@DineoKotjomela Месяц назад
Ma mafia ati😂😂😂
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Ndalamq zathu misokho yutha ukupeleka kwazigawenga azipha azibale anthu osalakwa Chakwera sukuwina ase ndakuuza
@DineoKotjomela
@DineoKotjomela Месяц назад
Ma mafia 😂
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx Месяц назад
Ng'ona zalusa kufuna kusaulisa Malawi
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Месяц назад
Malawi akulowera kuti abale? Long live the DC
@Pangolinimw
@Pangolinimw Месяц назад
The DC 😅😅😅
@adzonzicomedy
@adzonzicomedy Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Месяц назад
Ayi zikomo
@Leo-fj6gz
@Leo-fj6gz Месяц назад
😢😢😢😢😢
@JamesAlinafe
@JamesAlinafe Месяц назад
Tha DDDDD ccccccccc
@RitaKainga
@RitaKainga Месяц назад
Ulemu wanu the DC
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Месяц назад
The DC ❤❤❤
@user-rs7vx6hc1k
@user-rs7vx6hc1k Месяц назад
Koma what is the use of our currency in Zambia? I don't understand this.
@BlessingsMikeyasi
@BlessingsMikeyasi Месяц назад
Nazoooo
@WilliamKawaza
@WilliamKawaza Месяц назад
Tell them DC
@AnnastasiaChakwiya
@AnnastasiaChakwiya Месяц назад
Ai zikomo achakwera
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 Месяц назад
Ya balance 😢 RIP SKC
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Chili chonse chingowululika kumwamba kulandire ulemu
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Месяц назад
Mr Bon Kalindo ndinu oyankhuliradi a Malawi tonse, keep it up the DC.
@BornfiyesignalSignalmtema
@BornfiyesignalSignalmtema Месяц назад
The dc
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Месяц назад
Komanso chibadwireni ine ntchito ya asilikali athu muno mu malawi sindikuiziwa, chifukwa ngati nkuteteza dziko .bwezi atalipanga boma ili held responsible pa nkhani iyi infact predent akadamuchosa.
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no Месяц назад
Kukuyu nyamayake
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Месяц назад
Born kalindo 🙏🙏🙏🙏🙏
@katalamajames4947
@katalamajames4947 Месяц назад
Koma keni nsonda amadya mutu nkhope the same sekeleton ma R. V.sakugwira nchito
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Месяц назад
😅😅😅😅😂😂😂mankwala anapima sakugwila 😅😅😅😅😅😂😂😂yomweyo galu iwe
@user-jn7bt1uy5s
@user-jn7bt1uy5s Месяц назад
Zovetsa chisoni 😢
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
Choka iwe mbuli zokhazokha zomwe ziimakunvera iwe gawanani ndlmazo paja ndiyo ntchito yanu 😂😂😂mwayi ndi MCP ukudya bwino kamba ka mabodza akowo azipani akumakulipila 😅😅😅uziyamklika wamva
@tingamasi106
@tingamasi106 Месяц назад
Mbuli ndiwe mavuzi okhwimawo
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Месяц назад
Iwenso ndiwe galu,chitsiru
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Месяц назад
@@Dysonkhofi fisi,chule,mbuzi,,bulu munayiwala zimenezo zikomo God bless you 😊😊❤️❤️❤️ work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
@ednakaluwa5414
@ednakaluwa5414 Месяц назад
​@@user-bd5kw8oq1rutukwana anzako..opanda chifukwa ena akubwexera utchula dzina la Mulungu shame on you.
@ednakaluwa5414
@ednakaluwa5414 Месяц назад
Vuto u need attention
@AndersonChimwala-hz4so
@AndersonChimwala-hz4so Месяц назад
koma amalawi
@user-lc3sw8iz2g
@user-lc3sw8iz2g Месяц назад
Balance
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Месяц назад
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC 🤔
@kelvinsibande8779
@kelvinsibande8779 Месяц назад
The DDDDDCCCCCCC
@LiamTennessee
@LiamTennessee Месяц назад
Amazalandila malipilo a ntchito yomwe adagwila
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Месяц назад
Mmmmm haa?
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 Месяц назад
ANTHU PANO MMANGO PANGA MA COMMENT KOPANDA KUSATILA ZINTHU . NDALAMA ZOMWE ZAPEZEKA KU ZAMBIA NDI ZAMAYIKO ANGAPO KUPHATIKIZA MALAWI ANTHU OMWE APEZEKA NAZO NDIZINKA ZA KU RUSSIA OMWE AKUPANGA MA BUSSINES A MA DRUGS OSATI ZOTI BOMA AYI MMM KALINDO ECHI BOZA LENILENI ZINAMIZA ACHILOMWE AKOWO
@TysonMwenye
@TysonMwenye Месяц назад
Ndiye anthu aku Russia wo angapeze ndi ndalama zathu chifukwa choti akugulitsa ma Drugs? Ifeyo tikamapita ku mayiko akunja timasintha ndalama zadziko lomwe tikupitako.Ndipo tikamaliza business yathuyo tisanatuluke mudzikolo timasinthilatu zamalawi.Ndiye awowo apezeka bwanji ndi ndalama zathu (Mwk) koma kudziko lina chinawakanikitsa kusintha kumalawi konko ndichani ngati ndizachilungamo ndalamazo
@tingamasi106
@tingamasi106 Месяц назад
Ndalama zama drug mpaka sealed? Iwe ndichimbutumwa wamva
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Месяц назад
Kusonyeza kt zomwe zikuchitika dziko muno iwe zikukusangalasa et i uzaziwona ukazakwatila ukasiya kudyesedwako mbudzi yamunthu iwe kape
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x Месяц назад
Kape iwe
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 Месяц назад
mbutuma ndinu osaziwa zinthu alomwe matama basi tiyeni uko . mleke kutivuska mngalamuliraso yai chalo ichi jiiiiiiiii peter wanuyo no
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz Месяц назад
Ma 20kwachawooo??
@MinhoMasanza
@MinhoMasanza Месяц назад
Yah ndima mk20 koma each carton contains more than a million
@hudycorex1893
@hudycorex1893 Месяц назад
Mk20 Sindalama????? Iwe ndendiopepera bwanji!!!
@rhodricksalima5387
@rhodricksalima5387 Месяц назад
Paliso ma 5 pin tu
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz Месяц назад
Opepela ndi amako
@user-si8vm5vj8s
@user-si8vm5vj8s Месяц назад
Shame on you chakwera
@warrenmwambazi8342
@warrenmwambazi8342 Месяц назад
Very bad 😊😊😊
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki Месяц назад
Kalindo ndi nyatwa auze zitsiru izi.
@DineoKotjomela
@DineoKotjomela Месяц назад
Ma mafia 😂
Далее
ACHEWA AKU DOWA ASAMBWAZA EE!!🙌🙌
18:10
7 Days Stranded In A Cave
17:59
Просмотров 52 млн
Gli occhiali da sole non mi hanno coperto! 😎
00:13
BON KALINDO  LERO PA 17 JULY 2024 |
18:32
Просмотров 26 тыс.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 162 тыс.
BON KALINDO & JACOB AT DISASTER COMMEMORATION
10:44
Просмотров 309 тыс.
7 Days Stranded In A Cave
17:59
Просмотров 52 млн