Тёмный

Limpopo iiiih! ma demo ajatu kwabwela anthu akunja kudzaletsa atapangidwa hayala Ntanyiwa waulura 

Malawi Trends TV
Подписаться 30 тыс.
Просмотров 24 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

4 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 99   
@ShaolinThomas-ow8yn
@ShaolinThomas-ow8yn 12 дней назад
Inuyo mulungu adzingokuonjexelani moyo wautali basi ,chifukwa mukutimvetsa kukoma
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 11 дней назад
Asilikari anthu ntchito yao ndi kuchinda mahule mutchesi umu😂😂
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 11 дней назад
Umwa chani
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 10 дней назад
umakwana mtanyiwa tikuziwa zambili amalawi ambuye azikupasani moyo wautali 🎉🎉🎉🎉
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 12 дней назад
We won't fear anything even as Zambian s were coming in Malawi guys to fight that evil man chakwela
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 12 дней назад
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa.
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 11 дней назад
Akulu akulu mukulankhula koma sitikumva 😢
@JuuuKomba
@JuuuKomba 11 дней назад
Koma iweyo pokhapa pot awagwila ndakuimikila manja mwamba athuo agwidwad
@UsenLashid
@UsenLashid 11 дней назад
Komaso Mr ntanyiwa musalore Kuti anthu 8 amene agwidwawo asatuluke Ayi kufikila chakwela atule pansi udindo komaso dziko la South Africa asawapange rilizi Ayi kufikila lamampho atamuzenga mulandu chakwela
@WatsonNtchito
@WatsonNtchito 10 дней назад
Mademo akayambire kumamfumu hotel komweko tiyeni tonse tikasokhane popo pa mfumu hotel ku ma room achulidwawo osaopa
@user-ht7vs3dp2u
@user-ht7vs3dp2u 12 дней назад
Ntanyiwa iweyo ndi number one radio yako timainyadira kom athu athawa ziko lili rawo kom kumeneko moto kuti buuuuu mumtimamo angokhuta mphuma lokhalokha km mulimba Ntanyiwa woyeee
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda 11 дней назад
Akatula udindo chakwerayo, azibale ake onse azachotsedwe ntchto. Galu watitopetsa
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 11 дней назад
Asilikali a ku Malawi ndi ogona tulo zitsilu zimalimbana ndi anthu wamba usayelekeze kuvala kabudula wa makaka ndiye amaonesa mphamvu zawo ati wavala unform yawo mbudzi
@PeterMphanza
@PeterMphanza 6 дней назад
Nice job comred mwana wa amama kuno ku Zambia
@Hassankazembe-d3o
@Hassankazembe-d3o 11 дней назад
May God bless you comrade Ntanyiwa
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 11 дней назад
Koma chakwera wandikwana one day ndi kupedza people they call gringo
@BitonFred
@BitonFred 9 дней назад
Anthu akumalawi umbuli, anachotsa peter, ati wabwino chakwera, pano akufuna peter yemwe uja, mmalawi wanzeru sakuyenera kupeleka vote ku president yemwe analephera kale, votelani atsopano osati apeter muthalika
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 12 дней назад
Pano malawi ndi North Korea 😭😭😭
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 11 дней назад
Apapa ndatanganidwa kuwerenga nkunvesera😂😂
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 11 дней назад
Anthu nonse amene mukudana ndi nthanyiwa mitungati zoswera malambe inu zikukusangalasani mmene akuyendesela dzikoli gule wanuyi achoke alibe phindu
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 11 дней назад
Ankolo ku malawi kulibe a silikali akanakhala kuti alipo zikuchita galu ameneyo mukumuti chokwerayu atamukhazika kale pansi, koma nawo asankha kugwirantchito ndi chipani ayiwala makamulo awo ndi mbuzi za silikali za manu pansi ndi mbuyao chakwerayo tionana chaka cha mawa onse amene akupha ndi chakwera tikhaulitsa boma ili lapita olo ataopseza motani zosatheka
@CadTafa2
@CadTafa2 12 дней назад
Apolici a malawi a kuzishipisa
@misoMoyo
@misoMoyo 11 дней назад
Limpopo FM ineyo ndimachedwa Ku ntchito kuti ndimvere basi nkhani ZANU mumandidalitsa ine ndi m,ngoni weni weni more fire inuyo a Mr Ntanyiwa
@blacksonpeshes5057
@blacksonpeshes5057 11 дней назад
kom mukutivetsa kukoma ndikapanda kuva uthenga kuchokela kwainu sindipuma bwino kod mudarikuti mosemunja
@DuntumaziyaDuntumaziya
@DuntumaziyaDuntumaziya 11 дней назад
following you sir
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 11 дней назад
Kuti muone ku mcp kuli anthu osaoneka bwino okhaokha pamaso ndionyasa ndi mtima momwe
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 11 дней назад
Comredy mtanyiwa tikufuna number yanu tizipephela Nanu mulungu azikudalisani kwambili ndipo azikutetezani kulikose komwe mukuyenda
@user-vu4cz1mt4f
@user-vu4cz1mt4f 11 дней назад
Tisayembekezere kuti tingamve munthu wakuphayo kuti ndine ndapha mayz ? Munona kt wakupha kufufuza chifkwa chomwe wina wafera koma atapha ndiyeyo ? Mayankho ndiomwewa omwe tikumayankhulawa coz action ikuchitatu kuoneka yokha ndipo mwachindunji monga kumangidwa anthu then kulowesa zigawenga nde ngt akusakidwa anthuwa kuti aphedwe nde nkumat ena omwe adafa aja anafera zina ?
@PartsonMdeza
@PartsonMdeza 10 дней назад
nkhanga zaonaaa
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 12 дней назад
❤Zowona acc muthu ameneyu AChoke
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 11 дней назад
Ndipo chakwera tidzachita kuotcha pamoto chifukwa chankhanza akuchitazi
@JaneLikome
@JaneLikome 11 дней назад
Nice mr ntanyiwa
@stanleychisasa4343
@stanleychisasa4343 11 дней назад
Boss mbuyomu munatiuza kuti athu aku German ofufuza ndege aja anali okonza miseu lero muti ndi aku butcher which is which Big man?
@AugustineIshmael
@AugustineIshmael 10 дней назад
Zachamba basi dikilani 2025 vote yanu ndiye nuclear power osati zabibi zanuzi
@MikeMerecah
@MikeMerecah 11 дней назад
Ma activists athu musakhare chete kunoko akumangidwa mwachisisi mudziwe zimenezi, anthu osatchuka panopa Ali ku area 30 guyz,
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 10 дней назад
Ntanyiwa woyeeeee
@AjibuTwalibu
@AjibuTwalibu 11 дней назад
Umakwana ya mtanyiwa tili nawenawe my brother
@NisharChibisa
@NisharChibisa 12 дней назад
Mumakwana
@JamesIsaac-zi4kb
@JamesIsaac-zi4kb 11 дней назад
Chakwela ofuna adibwe kanyenya basi
@YONA-v5o
@YONA-v5o 12 дней назад
Anthu amenewo ngat agwidwa aphedwe ndinthu cifukwa iwowo anabwela kuzapha
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 12 дней назад
😂😂😂😂😂 zabwino zonse wachita bwino wagwidwa tiakonzere konkuno
@maluli5691
@maluli5691 11 дней назад
Asilikali Aku malawi ndi asilikadzi.west Africa asilikali sakunyengelela kulanda boma
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 11 дней назад
zinamizanani pano pa limpopo kwachwera ali pheee kukozanyasi zomwe inapanga dpp . alikuti anthu omwe agidwa aaa opusi mtanyiwa
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 11 дней назад
Iwe mutuwako suyenda ngati akutuma a mcp anthu akufinya ndi chakwera wakoyo ngati akupasa ndalama ulibe manyazi wekha otsutsa pano aaaaaaaa ona kolowera
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 12 дней назад
Hahaha AAA, Malawi poison party, Wanthu anawa votera dala, bolani ife tiri kutali zina ukamva zina Leku kamba anga mwala.
@jangiya03
@jangiya03 12 дней назад
Ambuye tithandizeni Malawi waipa
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 12 дней назад
Zoonad amalawi azimai tizingoyang'anira nyasizi bvuto azimai timatengrka ndi kathu kochepa
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 11 дней назад
Chakwela ndikanankhala kuti ndimatha ufiti ndinakamchosa ineyo manyi akee anthu
@EllenPhiri-xt8pt
@EllenPhiri-xt8pt 11 дней назад
Chitsilu chichakwela ndi family yake yonse ambuye tichotseleni munthuyi😊
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 11 дней назад
mademo mpanga komweko ku lilongwe ayi mkanya
@IssahAluba
@IssahAluba 11 дней назад
Chonde AMalawi asatiphimbe maso BOMA ilili osalivera tiyeni pansewu week yamawa osaopa gayz 💪💪🛶🛶🏹🏹⚒️⛏️
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 12 дней назад
Malawian kuwopa too much that’s why amakonda kulepheresa mademo so don’t tell us ngati muziwona zoti sizingatheke zochita mademo! Aaa why amakonda kulepheresa mademo
@BitonFred
@BitonFred 9 дней назад
😂😂😂😂
@walesbanda4959
@walesbanda4959 10 дней назад
😂😂😂
@MandalaChaona
@MandalaChaona 12 дней назад
M C P -- Malawi Congress Party M C P = Malawi Chikangawa Party 👹👹👹🔨⚒️⛏️
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 11 дней назад
Nde inu mukuganiza kut olo patabwera peteryo zinthu zingasinthe foundation ya Malawi kuvuta konseko ndi chipani Cha udf olo mutatani Malawi sazasintha
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 12 дней назад
Limpopo FM ndi 1
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 11 дней назад
Ukanakhala kut mwina ukutiwuza munthu wozamuvotera koma nawenso ukumpangila peter kampen choti uziwe peter nayenso atatitopesa kale sitikunfunanso
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 12 дней назад
Koma Malawi walowa chibwana chakwera anapita ku sukulu koma?pano akusekedwa ndi anthu akunja omwe
@HappyMaolid
@HappyMaolid 12 дней назад
It's time to figh now,osagona
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 12 дней назад
Chakwela ndigalu kwabasi
@user-xi2vo4gc4u
@user-xi2vo4gc4u 12 дней назад
Ku Malawi aku shooter ma movie rekani amenyane
@FrankMulela-qt1wi
@FrankMulela-qt1wi 12 дней назад
Number yotumizila zinthu kwantanyiwa plz
@SeephyMfaume
@SeephyMfaume 12 дней назад
MCP Pamtumbo pawo ndithu
@user-td6qe4gr6w
@user-td6qe4gr6w 12 дней назад
Chopweteka kwambiri ndi choti ndalama za nkhani nkhani zikuthela kulipira anthu a kunja amene zomwe akuchita mudziko lathu phindu lake opindula ndi ochepa
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 11 дней назад
Ndipo kwambili eni dziko kumangosaukirabe
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 12 дней назад
Koma chakwera anthawa wauyouyo mbwiyache.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 12 дней назад
Asilikira akumalawi ndi wopusa.
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 12 дней назад
If what comrade is saying is the truth,then Chakwera must be the worst president in Southern Africa.
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana 12 дней назад
8:30 musova mcp ,mulithawa dziko mukulifuna
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE 12 дней назад
Ndichoipadi ichi chigawenga chabechabe
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 11 дней назад
Mcp mukali kuyalukirayalukiratu
@EllinaBitto
@EllinaBitto 12 дней назад
😢😢😢😢😢😢😢😢
@UsenLashid
@UsenLashid 11 дней назад
Kodi inu apolice ndi asilikali ntchito yanu ndi chiyani kumalawiko? Kodi mukuyang'anila zika Zanu zikuphedwa Kodi inu ndinu apolice opanda ntchito pamodzi ndi iwe wa mkulu wa asilikali utule Pasi udindo coz your usiless man dammit asilikali inu achilungamo menyani nkhondo please
@CharlesMateya
@CharlesMateya 12 дней назад
Following
@dorisbutao4227
@dorisbutao4227 11 дней назад
Mmmh
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 12 дней назад
Atanyiwa pathako pako
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 12 дней назад
Yess
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 12 дней назад
Zowonadi mchutsuludi chimenechi
@user-yc3ik9dq3x
@user-yc3ik9dq3x 12 дней назад
Inu amenewo mungodziyankha nokha muli phee kugwiritsidwa ntchito ndi agaluwo 🥺mxieuw
@mipeacemakermw9501
@mipeacemakermw9501 9 дней назад
Mwatukwana president 🤣🤣🤣🤣ru-vid.com/video/%D0%B2%D0%B8%D0%B4%D0%B5%D0%BE-WRDkQ8s_34k.htmlsi=PkGoYsuJRKSW0v4p
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 12 дней назад
Chakwera atha ngati Idi amin sizimuthera bwino ndithu.
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 12 дней назад
Am waiting good news not bad news 😔😔😔😔😔
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 12 дней назад
Ndikut mambodza akowa Pali ine no comment ndizopusa zakozo tithana phwanga galimoto uma user ija nditha kukutumizira komaso pachikwangwani umakonda kucheza paj okay
@victorauwana7258
@victorauwana7258 12 дней назад
Mwapemphedwa kutu mupange comment?
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 12 дней назад
😢
@SoundmasterElectrical
@SoundmasterElectrical 12 дней назад
Mbudzi iwe uthana ndindani usawone ngat ndife ogona wamva panyo pako
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 12 дней назад
Chigawenga iwe chimunthu chopanda phindu chitsilu ulibe manyazi mulungu akukanthan
@LukaThawe
@LukaThawe 12 дней назад
Anthu achoka Kuti iwe nawendimbuzi kwambiri ukukofuna kusokoneza amalawi ,chifukwa amalawi ndiopepera kale ndiye azikuvera nyasi zako sata yako
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 12 дней назад
Muyiyambe muwone utsi ntanyawa Ali kunja athawa ataba mbuzi kumalawi
@user-tm3zh5zk4t
@user-tm3zh5zk4t 12 дней назад
Paja ninakuwuza kale kuti upite kumalawi mabodza akowo mtanyiwa yiweyo niamene ukumasokoneza anthu infe timapeleka ulemu kwa boni kalindo osati mbuziyiweyo ayi
@AchinaKellz
@AchinaKellz 11 дней назад
Achakwera vomelezani😂
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 12 дней назад
Chikamabodza chabwela zotani kukamwa ngati manyi
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 12 дней назад
Pain MCP
@user-yc3ik9dq3x
@user-yc3ik9dq3x 12 дней назад
Dzidyani za magazizo. Mulungu akulangani nkhuku inu
@AminahMussah
@AminahMussah 11 дней назад
ukatelo watumidwa nda nzako akuphawo
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE 12 дней назад
Ndichoipadi ichi chigawenga chabechabe
Далее
Зачем он туда залез?
00:25
Просмотров 250 тыс.
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
Просмотров 38 тыс.
KAMLEPO KALUA KUYANKHULA MOSANYENGELERA
29:23
Просмотров 40 тыс.
Зачем он туда залез?
00:25
Просмотров 250 тыс.