Тёмный

Limpopo mmh kwaipa anavula a Chilima lamba ndi ndani poti ndege singapange zimenezo Ntanyiwa uku 

Malawi Trends TV
Подписаться 29 тыс.
Просмотров 47 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

28 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 130   
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 15 дней назад
Munthu amene amadana ndilimpopo ameneyo ndifiti
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 10 дней назад
Yotamba 9 koloko mmawa 😂😂😂
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 14 дней назад
The best fm ,,, listening from Botswana I can't wait ❤❤❤❤
@clairelewis5309
@clairelewis5309 14 дней назад
Comrade Ntanyiwa .God bless you,protect you,guide you and entire family. SKC soul im sure ukukuyanganilani Comrade ,and the entire Limpopo DJ's🙏🙏. Nkhanga zikungoyenela ziziona👀👀👀👁️. Uku tikusala kudya ndi kupemphela ,chilungamo chioneke ndithu. Limpopo 🎉🎉🎉🔥🔥🔥🔥🔥 moto kuti buu !!!!, 🔥🔥🔥
@RenaChikupila
@RenaChikupila 14 дней назад
Dzoooona osamalimbana nawo inu pangani ubwedzi ndmlungu osati munthu odzuza thupi ndyesu yekha oteteza lnuyo antanyiwa❤❤❤❤
@ThokozaniSaiti
@ThokozaniSaiti 13 дней назад
Ndege munthu ndiyomwe inachita iziiiii Anthuwatu akuona ngati amalawi tikadali ntulo sakudziwa kuti tinachangamukaaa Muzionaa ndipo muyankha mafuso onsewa kwa amalawi and to the whole world Mfiti Chakwera
@PatrickMailos
@PatrickMailos 15 дней назад
My best ❤ Limpopo FM radio
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 14 дней назад
Inuyo ndi one ndpo sindmafuna pazidusa one hour tisanakumven mau nice big man
@augustMag
@augustMag 14 дней назад
The best Limpopo FM radio station is the one 🔥🔥🔥🔥
@user-sh5wq4uf6r
@user-sh5wq4uf6r 15 дней назад
Ntanyiwa komaso bakili muluzi these guys i salute 💪
@FisherAction
@FisherAction 14 дней назад
Mulungu akukuteni kut onyansa mtima awa osowa umunthuwa
@FisherAction
@FisherAction 14 дней назад
Asamakufikireni komano big tawakumbuseni a DPP Asiya uchetewawu adzuke
@EllinaBitto
@EllinaBitto 14 дней назад
Akutimenyera nkhondo anyamata awa amphawife😭😭😭😭😭😭😭
@user-zj1xx1ic2m
@user-zj1xx1ic2m 15 дней назад
Listening from cosmo city, just here malibongwe drive south Africa ❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉 Comrade!!! tili limodzi apa✅✅✅🇲🇼💪💯
@user-dy5bj9ck5e
@user-dy5bj9ck5e 14 дней назад
Congratulation Mr mtanyiwa gp🎉❤❤❤
@eunicesaiti
@eunicesaiti 15 дней назад
Limpopo following 🙏 SKC and others who died Rest in Eternal Peace 😢😢😢
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 15 дней назад
Pheee,pano pa limpopo ndi comrade mtanyiwa
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 дней назад
Ntanyiwa katundu owopsa zedi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-tm3zh5zk4t
@user-tm3zh5zk4t 14 дней назад
Iwe ulingati m,zimayi mabodza umangoduladula nkhani osayimaliza kuchita kudziwika kuti ndiwe wamabodza iwendiwe galu wachabechabe nakutuluka
@SaulosMbuna
@SaulosMbuna 15 дней назад
A Ntanyiwa chifuwa SI chipha osatekeseka..imwani madzi ochuluka
@stanleychisasa4343
@stanleychisasa4343 15 дней назад
Chairman ndinga pange bwanji ndizikutumizilani khani
@StellaCharles-dq8db
@StellaCharles-dq8db 14 дней назад
Tikusatira mwachidwi ndinthu ndipo alimpopo mukat musatumize uthenga ndinadandaula kobas andi bon kalindoso ulemu wanu pitizan kuima pachilungamo mulungu alinanu nonse mudzina layesu mulungu wamoyo
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
Were in Zambia but our hearts our bleeding
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
Masowela aaah yoooo timbwela from Zambia
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
I can't believe it that our brother is gone just like that No No
@TawongaGSMwale-cc2vm
@TawongaGSMwale-cc2vm 15 дней назад
Thanks for your update Big Baba
@JOHNMPEMBA-p3i
@JOHNMPEMBA-p3i 13 дней назад
I ❤ Limpompo fm
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 15 дней назад
RIP SKC, kodi nanga anthu 8 enawo imfa zawo zinali zotani? Pamenepa sipakumalongosoredwa Mukhale ndi moyo wautali comrade ntanyiwa anthuwo angodana nanu akusowa zochita chifukwa mumanena chilungamo
@GiftPhiri-tt7nn
@GiftPhiri-tt7nn 15 дней назад
Ngati chilima anaphedwa ndiye kut onse anaphedwa , kaya ndingozi ndiye kut onse ngozi eeeeetu
@FocusMind-nj8gy
@FocusMind-nj8gy 13 дней назад
More fire
@IssahAluba
@IssahAluba 15 дней назад
Limpopo FM 💪💪
@user-zj1xx1ic2m
@user-zj1xx1ic2m 15 дней назад
Ndiponso chigwada chake chimakhala chosinja kale😂😂😂 Mr ntanyiwa mumayidziwanso Randburg????😂😂 I love u Mr mumakwana Enawa ndi Ana awa❤❤❤🎉🎉🎉
@alicehananiya
@alicehananiya 15 дней назад
Listening 🎧 from springs
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 9 дней назад
Antànyiwa amwalila pangozi yangalimoto
@JelemayaMagugu
@JelemayaMagugu 15 дней назад
Bwana timakukondani ndipo timakunyadirani chifukwa mumatidziwitsa chirichose
@tlhalosozindlani4544
@tlhalosozindlani4544 15 дней назад
Hehehehehe yomweyo galu iwe awuzeneni amvese comred ntanyiwa
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 11 дней назад
Tafunsidwapo kale kuno ku south Africa za imfa ya chilima
@ChisomoChalera
@ChisomoChalera 15 дней назад
Timakunyadirani alimpopo fm
@EfeloYovita
@EfeloYovita День назад
kumwanza ndikwathu mulo nde ndani ife or dausi sitikumufuna
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 9 дней назад
Antanyawa atisiya pangozi yagalimoto zachisoni
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 9 дней назад
Antanyiwa atisiya😂😂😂😢
@user-yi2fg1lh8x
@user-yi2fg1lh8x 15 дней назад
Listening from randburg..
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal 15 дней назад
Same to me
@FisherAction
@FisherAction 14 дней назад
Mmatiimirira bwana
@isaaczuze
@isaaczuze 12 дней назад
Kkkkkkkkkk koma ntanyiwa kkkkkk usandisekese apa ....redson munlo mutu wake siumagwila olo mpang,ono pomwe ......anamangisa ukwati mamawa pofika madzulo ukwati watha ..naperi seventh day kunaperi ku blantyre ......redson munlo ndi chisilu cha munthu
@davidjames679
@davidjames679 14 дней назад
limpopo fm ft bakili muluzi tv 🔥🔥🔥🔥
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 13 дней назад
Limpopo ndekuti chani
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 13 дней назад
Mbambande Limpopo
@JonathanZiba
@JonathanZiba 15 дней назад
Ndikangolowa pa RU-vid choyambilila ndi mafuna ndi mvele Limpopo fm koma ka melody mumaikaka kamatalika kwambiri musanayambe kulankhula ofcourse ndika bwino koma kasamatalike kwambiri nthawi Zina timakhala tili pachangu nde kamatipangisa kuti tisamalize kuvela
@PatrickKabwinja
@PatrickKabwinja 15 дней назад
Vgg🎉
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv 15 дней назад
Limpopo to the world 🌍
@DoreenEmmanuelj
@DoreenEmmanuelj 14 дней назад
Congratulation mr mtanyiwa❤❤❤
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 15 дней назад
Ma demo akanapanga pa 20 coz ana pa 10 akhalabe akulemba mayeso
@user-zl9eq8jw1q
@user-zl9eq8jw1q 3 дня назад
Ndege mpakana kuvula tie mmm
@josephkuseke4166
@josephkuseke4166 13 дней назад
Ku Randburg ndinapezako mbewa ndi ngumbi
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 14 дней назад
Kkkkkkkkkkkk yochita zonsezi ndege yomweyo? 😂😂😂😂❤❤🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@user-hs2dw7ly2c
@user-hs2dw7ly2c 5 дней назад
Mcp ndi leadership wawo Chakwera ndi galu kwabasi
@MwasamboMwasambo
@MwasamboMwasambo 13 дней назад
Nkhani zodabwitsatuu iziiii
@RhaudanRhaviwa-i8b
@RhaudanRhaviwa-i8b 15 дней назад
Nthanyiwa umakwana timakunyadila MCP ndiyamagazi mmaja kuyambira kale
@user-ir2yz5zz5x
@user-ir2yz5zz5x 14 дней назад
Chobisika chili chose timavera kuchokera kwa limpopo FM kuchokera kwa khomuredi Ntanyiwa mumati vesa kukoma kwambili ndpo timaku pephelerani kwambili ndpo oyipayo sangaku kwaniseni kt akupangeni chipogwe ndpo mulungu apitilize kukutetezani mix born kalindo mulungu apitilize kukusungani ndimoyo wautari pa libe radio iliyose yomwe ingatiuze zoona zokha zokha ndi limpopo yokha bas mulungu apitilize kukumenyerani khondo nose
@user-fh1nc3kf2r
@user-fh1nc3kf2r 14 дней назад
Limpopo ndi namber one
@NdazionaSasu
@NdazionaSasu 14 дней назад
Mbambande mtanyiwa❤
@Robertmkango
@Robertmkango 15 дней назад
Limpopo tiziwiseni munthu ama munkhapa chilimayo timuziwe
@Jamesmwale-iz4ri
@Jamesmwale-iz4ri 14 дней назад
Tikutsatila mwachidwi
@JhdaLifi-vu9sd
@JhdaLifi-vu9sd 15 дней назад
A chair man
@user-ml8lk9dr7t
@user-ml8lk9dr7t 14 дней назад
The problem is that ayesetsa kuti akuchiteni chipongwe koma alephera anthuwa Comrade ndiye nzeru zatha
@Jaydee-mw4
@Jaydee-mw4 15 дней назад
Yes anawavula ndani?? Poti ndege ilibe manja 😅
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 15 дней назад
Bwana Mtanyiwa gwirani ntchito Basi osalimbana ndizinazi zikuiwalitsani zochita
@SmileMalanda
@SmileMalanda 15 дней назад
Ndipo inuyo munasowa😂😂😂😂
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 15 дней назад
NTANYIWA MBAMBANDE , KOMA VUTO NDI ROTI MAFUMU NDI ANTHU ADYERA KOMASO MA BISHOP MITUYAO SIGWIRA NTCHITO, NDIPO MAFUMUWA AKUFUNIKA KUWAGWIRA PAKHOSI KOMASO MA BISHOP NDI ANTHU OTI SANGATHANDIZE DZIKO CHIFUKWA MWAIWO U MULUNGU MULIBE MWSIO MEADZAZA NDI DYERA MALO MIYANG'ANA DZIKO MOMWE LIKUYENDERA NAONSO.TIWAPANGIRA MADEMO NGATI SAKUDZIWA ASATIONONGERE DZIKO CHIFUKWA CHADYERS LAO IYAAAAAA
@boldmovesafrica4551
@boldmovesafrica4551 13 дней назад
Hand mistake sorry I want to press like ❤😂
@FredKanyerere
@FredKanyerere 14 дней назад
Limpopo mumakwana from Cape Town
@EllinaBitto
@EllinaBitto 14 дней назад
Mzimu wa Chilima itipatsanso hope ina mayooooooo ine A Chilimaaaaa😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@AudettaYohanie-fl3oc
@AudettaYohanie-fl3oc 14 дней назад
God pleasease,, protect ntanyiwa Abeg 🙏
@Mamahashim-xw2bg
@Mamahashim-xw2bg 15 дней назад
Ndipo mulungu azikudalisani
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 13 дней назад
Kodi photo ya a chilima yogwira kolona alipo angandionese?
@user-hg2cw1om1p
@user-hg2cw1om1p 15 дней назад
Limpopo FM❤❤
@user-qb2lt6qj1p
@user-qb2lt6qj1p 14 дней назад
Oyenela kupepesedwa ndi akubanja km chakwela anapepesa ndi 5milioni ndizovesa chison kt chakwela akugawa ndalama kwa anthu omwe malilo sakuwakhuza tichedwepo pamenepa
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 14 дней назад
Eeeeee imfa iyi ikupweteka ukailingalira, Ambuye kumwambako mumadziwa zonse😢😢
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 14 дней назад
Inetu ndi mathokoza kwambiri a Limpopo FM ndipo ndadziwa ndale chifukwa cha Limpopo FM pitirizani kutipatsira nkhani zonse mulungu adzikudalitsani bambo muthwanyiwa
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 13 дней назад
Tiuzeni inuyo munali mundegemo mukutifusaso ife
@user-lp7vd6nj9z
@user-lp7vd6nj9z 15 дней назад
Kkkkkkkkkkk koma zidyamula nandolo
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
Tizapindula
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 15 дней назад
Uyu ndi machine owopsa zedi Ntanyiwa❤❤❤❤❤❤❤
@user-zl9eq8jw1q
@user-zl9eq8jw1q 3 дня назад
Mafunso waponda mayankho atiuze bwino
@isaaczuze
@isaaczuze 12 дней назад
Koditu pagulupa pali zisilu zina zadya ndalama zokukuba ndiye asowa choyankhula ......mukuteteza anthu oti akukuzunzuni kodi ndalama akukupaanizo akupasani kangati .....chakwera akuchoka pavute pasavute ngati akakamire mmalawi muno mukhala nkhondo ya nyooooo .... Chakwera kumwela sazapita komanso kumpoto
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 14 дней назад
Akufuna ma vote a chakwela kuti mafumuwo akalimbikitse anthu awo akati tiyeni timvotele MCP
@MaryChihana-y4b
@MaryChihana-y4b 13 дней назад
Koma ndiye anthu awa
@WitnessMaulidi
@WitnessMaulidi 14 дней назад
TAnyiwa we are defending Malawi
@ClementbWatches
@ClementbWatches 15 дней назад
Iweyo Ntanyiwa ndi number one ndipo ndimamva nawe kukoma zed. Ndipo timamva zenizeni
@lawrencemalinda603
@lawrencemalinda603 12 дней назад
We salute you
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 15 дней назад
Koma nde Apengedi misala mwinanso anachita kuyitanidwa kuti atsekedwe pakamwa nkona adzibusa Mafumu ndi ena azipembezo zosiyana siyana akukhala phe kumangoyang, anila dziko likungowonongeka chifukwa chodya chibanzi Mulungu akulangeni nonse amene mukungolandila ndalama koma chilungamo mukuchidziwa Koma nde okapanga kidnap wo adzafera konkotu
@raphaelfanuel4608
@raphaelfanuel4608 15 дней назад
Ntanyiwa sing'anga amuka drip yamadzi atapita kukathamangitsa mizimu mwaterooo😂😂😂😂
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn 15 дней назад
Siziwona
@ZaccheousPetrol
@ZaccheousPetrol 14 дней назад
Khumbo la apolisi anthu komanso a army, ma doctors,amphuzitsi....its just better life not to be rich
@user-no2sn1fo1h
@user-no2sn1fo1h 15 дней назад
Rip our vp
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
We can't 10 July come one come all their see
@user-ml8lk9dr7t
@user-ml8lk9dr7t 14 дней назад
We are not young GOD is watching
@BenardMwale-cp7sy
@BenardMwale-cp7sy 14 дней назад
Following ine zanga phee mix lawyer ndilibe kkkkkk
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
Demonstrations a kulu timbwela better there tell us🌟 the 😭 truth why there killed our brother
@DoreenEmmanuelj
@DoreenEmmanuelj 14 дней назад
Missing dear ❤
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 15 дней назад
Apatsa Ambuyache mafiti opephera km mulungu awayendele
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 15 дней назад
This is sad for sure
@InnocentMasuli
@InnocentMasuli 15 дней назад
Umatha ase
@AbdulChitundu
@AbdulChitundu 14 дней назад
Mumakwana inuyo big
@Marymahendra
@Marymahendra 14 дней назад
That’s true Vs president he was going for funeral with suit and tie now he body is nicked so how take out his clothes is look like something that does happen, am very sorry what happened to him and died like thief and Chikwara he is proud like nothing happened
@TaongaDafter
@TaongaDafter 15 дней назад
Siwe munthu wamba adha umakwana
@user-cq3kb7ii8h
@user-cq3kb7ii8h 15 дней назад
Ndipo tisaladi kudyako chilungamo chioneke basi
Далее
BON KALINDO 15 JULY 2024 CHI MNG’ALURO CHA PA MONDAY
13:42
Minecraft Pizza Mods
00:18
Просмотров 791 тыс.
Сколько метров чернил в ручке?
16:35
Zamanyazi mukafukufuku  wanimfa ya saulosi chilima
5:45
Agula mfuti 400 kuchokera ku Israel zophera anthu
8:20
kumalawi kuno ndani wandale angamake??
1:01:32
Просмотров 75 тыс.