Mfumukazi fire fire Mabomba. Apapa Guys mwaipota ntchito Mbambande Mfumukazi. A Chitsime musadane ndi aliyense koma mudane ndi Khalidwe lanu lomwe linakuchititsani kuti Nagama atsale yekha, mukuyenera kuvomereza basi kuti Ndiwo zosavinikililidwa ndi zomwe mumatera Ntchentche ndipotu Ntchentche zake zimakhala zirizonse. Ndi chifukwa chake Jemason, Gututu komanso Padera amapita kwa Nagama chifukwa Nagamayo anali ngati NDIWO ZOSAVINIKILILIDWA
Good work!! Could you kindly assist me with these three episodes: 12/10/2022, 02/11/2022, 22/02/2023. If already uploaded please share the link. Kind regards