Mzimu wamunthu Uma usa bwino through chikhulupiliro cheke kwa Mulungu basi that's the best way,,koma ngati chikhulupililo chathu chosemphana ndimomwe Mulungu watilamulila mmmm basitu or ife titamukonda motani koma ndimavuto basi
Zoonadi abale otsogola saziwika paja APM adanena, ndunena izi chifukwa pakati pa Bambo Paul ndi Lucius amene amaoneka mupwetekerako ndi Paul komaso ndamene thandizo limapezeka mopuwala