Тёмный
No video :(

Tiyankhula Mpaka Tiwachose Mu Boma 

Mukuziwa?
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 16 тыс.
50% 1

#malawi #trending #viral

Опубликовано:

 

24 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 90   
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Месяц назад
Thank God to have brothers like him, kalindo, mtambo, Samuel rwala, bakili tv, ntanyiwa, ndi ena ambili chifukwa akuyimila ndithu
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Месяц назад
Salute comrade.... Together we can wake up malawi
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
More fire brother 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@kurhikhoza8298
@kurhikhoza8298 Месяц назад
Amen amachita m atha ndi modzi mwayiyo
@EllinaBitto
@EllinaBitto Месяц назад
Ma brothers awawa penapake akumatithonthodza za imfa ya Chilima😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@ElonBlack1999
@ElonBlack1999 Месяц назад
Our freedom fighter
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p Месяц назад
Zoonadi Brother
@hugoorthodontics4486
@hugoorthodontics4486 Месяц назад
Tikudikila
@user-hg2cw1om1p
@user-hg2cw1om1p Месяц назад
Inuso mwabwera ndiyabwino❤❤
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Месяц назад
🔥🔥🔥🔥
@anthonybato2972
@anthonybato2972 Месяц назад
Keep it up...
@OzzyFay-qq6by
@OzzyFay-qq6by Месяц назад
True brother
@amoschataika7440
@amoschataika7440 Месяц назад
True Son of Mw, big up Brother
@user-zr4vn4mb5z
@user-zr4vn4mb5z Месяц назад
More fire brother 💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-yi4oc4xz4v
@user-yi4oc4xz4v Месяц назад
We need that information
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
That's true bro, akhwakhwananda akuphawa ayiona game kuti yachema mkuona akuopseza kuti wina aliyense asamalankhule zokhunza imfa ya chilima, ayiwala zoti twitter siyawo, Facebook siyawo,watsapp siyawo, utube siyawo, Instagram siyawo, enuwake a utube akutumiza zinthuzi ndima video osiyanasiyana including chilima kwazungukoo!, nde iwowa ndindani kuti azitiwuza zochita ifeyo ndi utube ?, who are they?, who is peter kalaya?, who is daud suleiman?, they're bustards men!, mxiem
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq Месяц назад
SALUTE!!! FOLLOWING
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Месяц назад
I salute you big man
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Месяц назад
Tidikilira mwachifatse ndithu bwana
@user-hy6gc6ld9w
@user-hy6gc6ld9w Месяц назад
More fire fada
@justinphiri2025
@justinphiri2025 Месяц назад
Amenewa aziona tsogolomu
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt Месяц назад
Backward never forward ever keep it up.
@SolomonShaibuh
@SolomonShaibuh Месяц назад
We follow you
@LameckBanda-ph2nh
@LameckBanda-ph2nh Месяц назад
Big up father
@khadijailiyasa5315
@khadijailiyasa5315 Месяц назад
Bola lomanga anthu ati tiziopa koma zoonadi zimenezi 😢
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Месяц назад
You speak reality bro, But you know what , the best solution is only demonstration , only speaking that means we're not serious, we can't build our country by speaking . This government under tonse alliance is destroying our country and we're busy with noise ,
@fact-age
@fact-age Месяц назад
Same old MCP tactics to silence their critics. MCP leaders think we have short memories. We still have fresh memories of how the great sons of Malawi died, some of them even greater than Kamuzu, we still remember great politicians like Dick Matenje, Aaron Gadama, Twaibu Sangala, David Chiwanga, Orton Chrwa, Atatti Mpakati, Mkwapatira Mhango and many more. The courts cleared MCP, and its former leaders of these crimes that's why MCP is not scared to use their same old tactics to eliminate their critics as it is apparent to them that they will eventually get away with the crimes. The John Tembo imposed politician is another dictator and a mafia in the making. We need to take them out of the government before it is too late, before more lives are lost in detention, before more assisations take place. We have witnessed a suspicious plane crash already. We don't want any more politically caused deaths.
@HaspaSyed-zw4zi
@HaspaSyed-zw4zi Месяц назад
waiting
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim Месяц назад
100% my brother
@KenDuweh
@KenDuweh Месяц назад
Iwe unankhl kutali choling uzitiudza zoonad unachita Uyu chakwera uyu achoke basi
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Месяц назад
Thanks so much
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Месяц назад
True son of the soil Lwara akuyankhulira konkuno,zomayankhula muli muli mu bulangeto zi aaa
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere Месяц назад
Aaa zaziii inu munthu zoona akafuna kulankhula ayambe wachoka komwe aliko ndeabwere Ku Malawi kuno Kuti adzangolankhula basi? Tidzikhalani serious Koma mukamafuna kulankhula mudziyamba mwaganiza Kaye,Achina Lwara mukambawo Ali kumalawi kuno mchifukwa akulankhuliraso Ku Malawika
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 Месяц назад
@@ShabaniKuswere Auze zoona amvetsa umbuli wachuluka kwambr anthu amenewa
@ThokozaniBanda-cx7fw
@ThokozaniBanda-cx7fw Месяц назад
Umakwana bro
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Месяц назад
azako olimba mtima akulankhurira komkuno osati nyasi zakozo bwera uzayankhurire komkuno ndiwe ndani
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
Ndipo chilibe manyazi chikuwona ngati ku joni kuno ndi kwawo bwanji chikayime upulezident pachokha
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Месяц назад
Pa mbuyo panu bro chakwera watitopesa ife
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk Месяц назад
True son more far
@RomdakaJenningsSautie
@RomdakaJenningsSautie Месяц назад
Osaopa
@PatrickMailos
@PatrickMailos Месяц назад
Tipanga share
@PatrickMailos
@PatrickMailos Месяц назад
Topanga share
@tonyinocent1770
@tonyinocent1770 Месяц назад
Bigger up yourself
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 Месяц назад
Khad uli bho iweyo
@ajudyaustine984
@ajudyaustine984 Месяц назад
Chakwera must go if not 🇲🇼 will be lyk kenya
@user-vu4cz1mt4f
@user-vu4cz1mt4f Месяц назад
Ife Mantha tilibetu mesa ayamba kuluma APA kutanthauza mphamvu zawathera
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Месяц назад
Tiyeninazon bro atikwana anthuwa angotimanga bas ..phunziro ku Kenya mademo avuta onse pansewu
@DoreenEmmanuelj
@DoreenEmmanuelj Месяц назад
Mukumasowatu
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r Месяц назад
Kodi kurankhura rankhura kumasintha zinthu ngat munayambira kurankhura muja ndirit anzanu kukenya uko ukuswa pariyament inu bas deiry kumango rubwa rubwa ingo vomereza kt amarawi mavuto tanaazorowera bas
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 Месяц назад
Mumatha big mn
@user-ce8ud5ed5y
@user-ce8ud5ed5y Месяц назад
Umakwana
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron Месяц назад
MakApe osakonda dziko lawo
@BambordKabambe
@BambordKabambe Месяц назад
😂😂😂😂 kodi mutakhala inu boma mungatani😂😂😂
@user-vf2fo1mb2c
@user-vf2fo1mb2c Месяц назад
Yeah man, MCP nothing well
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Месяц назад
Ndipo tiyankhuka za imfa ya Chilima mpaka 2025 wooo
@nancynyirenda6774
@nancynyirenda6774 Месяц назад
Boma mukuliwononga nzeru mulibe Panga mwekha bwaji ukulankhulira kunja kwa dziko wosapita ku Malawi Kunene zoipa za dziko lako ndipakamwa pako Nzeru ulibe
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Tachokani apaa iwee, akhwakhwananda akupha inu
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Iweyo ndamene ulibe nzeru achokatu Chakwera okupha Chilima
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 Месяц назад
Ndipo ndi galu ameneyu bwanji
@PetroJack
@PetroJack Месяц назад
Phwala lako nyau ya MCP choka pano
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 Месяц назад
@@PetroJack Mwana otembereredwa iwe sukudziwa chomwe ukulankhula
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e Месяц назад
MUMATIYIMILA SIR
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI Месяц назад
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e Месяц назад
Ndimanyazi omwe alibe anyapala amenewa....
@hugoorthodontics4486
@hugoorthodontics4486 Месяц назад
Timve zenizeni basi
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs Месяц назад
Iwetu ulikutali ase
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Koma ndi Mmalawi akuyenela kuyakhula zakulhosi kwake MCP yakupha
@robenallie6985
@robenallie6985 Месяц назад
Ndiye ngati ali kutali
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs Месяц назад
@@Musa1828-l5d eya komatu MCP ikumanga athu iyetu sangamangidwe nao tisamale guys pa malakhulidwe dzikhali wayaka Moto ndikumanga
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Месяц назад
Chakwela anapha chilima
@graciouszgambo560
@graciouszgambo560 Месяц назад
Iwe ndichisiru cha munthu pita kumawalawi akakuponde azizako
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 Месяц назад
Tili limozi mcp yapita basi
@mzondinkosi1151
@mzondinkosi1151 Месяц назад
Bwerani chabe kuno big
@lawrencekananji7305
@lawrencekananji7305 Месяц назад
Komatu mvuto lake amalawi adzeru inu, olakhula kwambiri inu muli kunja kwa dziko lino. 😂😂😂 ndiye titani sopano. Of course mukunena za dzeru komano kuno sizingamveke bwino.
@SamJalie
@SamJalie Месяц назад
Ziribwino, mwina aziziwa kuti they cannot control all the accusers
@nancynyirenda6774
@nancynyirenda6774 Месяц назад
Ulibiretu nzeru iwe
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Ulibe nzeru ndiwe mwana wang'ona iwee, asatana okupha chilima inuu, tikuthotholani 2025 ndipo mukawolela kundende nonse
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Ulibe nzeru ndiweyo ukusekelela zopusawe galubwako fiti
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Месяц назад
MCP ndi ufiti
@AceelectricalengineeringAEE
@AceelectricalengineeringAEE Месяц назад
Ili kuti evidence kaa changu dhala
@PatrickMailos
@PatrickMailos Месяц назад
Topanga share
@OssmanAbubaker-st7pu
@OssmanAbubaker-st7pu Месяц назад
Zoonadi big MCP ndi Chipani cha kupha
@PatrickMailos
@PatrickMailos Месяц назад
Topanga share
Далее
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 50 тыс.
best way out of the labyrinth🌀🗝️🔝
00:17
Просмотров 2,6 млн
KWAPHULIKA AUDIO YACHILIMA MU NDEGE ISANAGWE. TAMVANI
10:45
BON KALINDO TTV EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BRIAN BANDA
3:00
Minyama yathu ngati amalawi ikuchokera pati?
16:31
Просмотров 63 тыс.
Malawi Music, LULU sings Palibe Vuto
4:47
Просмотров 386 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Zikhale Ngoma Kapena Drums?
10:46