Amatero anthu ndi Obama zimachitika Koma anthu akewo sakhalitsa ndipo imakhala plan ya asi Ganga amatenga ma information kwa anthu a pakhomo kenaka kumabwera gulu Lina mkumati ayi siwanu ndi wathu imakhala ma plan awo
Koma funso ndilakuti Kodi amene amati mzimaiyo ndi wawo ndipo ndi wamisala anachokera ku Dera liti ndipo mudzi wake odziwika ndi anthu a mmudzi omwe maiyo anamwalirawu?? 😮😮 This khani can't be understood easily unless one knows *Science in Witchcraft*