Can we give mtebe and belita their flowers 😂😂😂 their scenes are always fire😂😂😂🔥🔥 ayi ine matemba ndimawakonda ndie ndimafuna ndizidya atleast Ka 6 pa week lachi 7 masamba😂😂😂 this got me😂... komanso hyphen timufufuze amudyetsa kenakake😂😂
😂😂😂with that smile Gani amvekere "now its my turn"...targetting Albert's wife 😂 cholinga mumulandenso,mukufuna mzanu achite kutani ngat wachita kusiya mowa.... Chenkope a.k.a ashado atibulidwa liti ndi aichocho awadyera ndalama ya nyumba ya ena aja??
Guys inuo mumandiwaza eeeeh❤ ati ati mungogogoda ngat kwanu😂😂😂ati mufuna muzabe muli mbulanda😅😅 eeeeh koma Sangie eeee🎉🎉🎉ai zikomo......😂😂 henewe love you guys ❤🌼🖤