This is what Malawians were waiting to hear from you. You made a right decision. Thumbs up to you all. We are fully supporting you, and we shall be behind you forever.
This is practical and very positive politics. Let's follow this path. I never new that in UTM there are some pipo who think like this. There is so much unnecessary noise which pipo think is politics but nope. God bless you.
Ndinu mburi zedi mulipachangu koma choononga komaso kachipani kanu kakuntha nanga ku d p p mulibepo Udani a a a si wa UTM iwe ukufuna kuononga mpunga WA UTM
Samamva asiye adzaziona ayiwala zimene adamupangira mademo APM azabwezera zonse zija mmmn they have to learn through mistake with tose alayasi km UTM bwanji mwayamba kuti gwesa phwayi
Koma a mayi inu mutizuza kwambiri ndipo you have to learn through mistake muyambilaso tose alayasi tatopa ndi kuliratu ife Chaka chino Chigoliyati chinalephela khondo kwa David nde inu bwanji a UTM km DPP yanuyo 2020 munayipangila mademo nde mwayiwala km mukazi wa Loti adayang'ana m'mbuyo ndikusanduka chulu
Osamakakamiza aliyense ali ndi ufulu ndi chisakho chake pokavota. Panopo kuigwetsa MCP nkovuta aaaa nde gwirizanowo ndi dpp?? Mayi mukunama inu kuyakhula konseko ndi mpando musatinamizepo apa.
Inenso ndine wa pa kanthawi ndithu MCP ndayiwona ndipo ndimaidziwa. Kungoti zangovuta kt zipani zinazi ndizazing'ono nchifukwa chake people will be FORCED to make an aliance with DPP. Koma tikawunika BWINOBWINO, DPP ndi MCP palibe kusiyana. Njauju mkulu wa ACB dafa ngati simunthu mpaka pano milandu idangozizira. UTM tsaopano payokha itha/ ndi AFORD, zitha kuchita bwino ndithu chifukwa imfa ya SKC idachita CAMPAIGN YAMPHAMVU. Makamaka ku chigawo cha ku mpoto. Kubwelera ku DPP itakhala LAST OPTION, yes mwachonchi mowawidwa mtima. Mayi ndakumvani BWINO ndithu, ndipo sindikukutsutsani kwambiri, koma DPP, ikhale last option.
Paja DPP ndi kuchimake kwa Propaganda😂😂 Pepani a DPP the only new Malawi that as a nation we all expect is the coalition of UTM and AFORD period. We all all seek New parties in new Malawi to come. The MCP that Malawians have experienced this time NO majority can make such mistake to vote MCP again.
Mwaganiza mokhwima maganizo abale athu a utm kupanga mgwilizano ndi DPP komanso tili ndichikhulupiliro kuti zipani mwanenazo mosogozedwa ndi Ambuye komanso anthu kulilira dziko lamalawi pamene lafikapa liphulidwe pa moto osatira azipanizo sionse angakondwere koma ambuye achite kufuna kwake pempho a DPP zichepeseninso pa anzanuwo kondanani samaliranani khululukirananipangani umodzi ochokera pansi pa mtima may God bless you
Yes l gree with you Mai,koma ngati simungamve magnanimous a Maiyi ndiye kuti mulibe magnanimous ofuna kutumikila a Malawi koma kukhutisa mamba zanu osati kuombola aMalawi ku Bagamoyo,please paganism chtheka kugwilana manja kuombola Malawi ku mng"anjo ya moto,machine ngati achitila kuno ku south Africa kupanga boma la Malawi colution Government, osakonda anthu awo mwasiye choncho