Тёмный

Zaululuka kuti Chakwera wapha Chilima 

Jay Kawere Mw
Подписаться 7 тыс.
Просмотров 75 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 184   
@BridjetFrank
@BridjetFrank 21 день назад
Wayankhulawe yehova akukuyang'na pa khani imeneyi
@MwenyeCheNsoma-gb2yz
@MwenyeCheNsoma-gb2yz 21 день назад
Don't promote violence please
@Mpikamezo20-nt5dv
@Mpikamezo20-nt5dv 21 день назад
Kkkkk freedom of speech...from Mulanje
@MumbaPlayson
@MumbaPlayson 21 день назад
Condolences to you and the family.may the Grace of GOD be with you all.amen.
@user-tg3bl5ey9v
@user-tg3bl5ey9v 21 день назад
Koma akuyakhulawo siwangopeka coz mawuwo sakunveka mwa ndalama 😅😅
@DevidsamZikacha
@DevidsamZikacha 21 день назад
Ineyo ndikuona kuti m c p ingothetsedwa bass
@acklaschintowe
@acklaschintowe 21 день назад
Yes ayambe chipani china zoonadi
@jackiemayanika
@jackiemayanika 21 день назад
Isadzanvekenso mcp ipite ndi ma minister ankhanza onse asadzalowenso chipani chilichonse
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 21 день назад
Onse akwiya apa ndi A MCP okha okha tiziona
@user-lr2wx5xd9d
@user-lr2wx5xd9d 21 день назад
Muziwe kuti mcp basi yatha mwapita ndipo tikumangani
@LilyMbewe
@LilyMbewe День назад
Munthuyu akubisa voice yaku kkkkk
@thondoyaenterprise3795
@thondoyaenterprise3795 21 день назад
The beuty of freedom of speech 😂😂
@wilbroadm
@wilbroadm 21 день назад
Ndapanga subscribe,.you will update us more.
@JustinLipipa
@JustinLipipa 21 день назад
Kkkkkkk komatu guys muzikhala serious
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs 21 день назад
Koma iweyo momweukuvekela ungayakhule ndi apule ine Siwa MCP Koma idzizi ndidzazi!!!!!
@johnkambala692
@johnkambala692 21 день назад
Wait for investigation. Don't rush.
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w 21 день назад
Kuyankhula zosamveka ,AMalawi ali ndi njala yofuna kumva zowona zosatira za imfayi .So try kubwelesa zinthu zomveka kwa anthu 😅😅😅😂😂😂
@Wittie0505
@Wittie0505 21 день назад
Uyuyu ndiwabodza uyu😂😂 zochita kukonza izi😂
@MustaphaImuran
@MustaphaImuran 21 день назад
😅😅😅😅😅😅😅😅 Nyasaland ayi zikomo
@Donvaga
@Donvaga 21 день назад
Chizungu chakecho eeeee😂😂km guys mumathatu kkkk😂
@user-ty5wq9js8f
@user-ty5wq9js8f 21 день назад
My heart is totally broken due to Mr chilima's death, but I can see that this guy is lying. Uyuyu asatipusitse pano. Nthawi zina chilungamo chimadziulura chokha.
@user-zf9xs3zj9b
@user-zf9xs3zj9b 21 день назад
😂😂 Awa sanadye sizikuveka zomwe akuyankhula
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e День назад
Usakumva ndi iweyo ambiri tikumva ndipo zamveka bwino
@enockdaisi1306
@enockdaisi1306 21 день назад
Aaaaaa choka iwe nawe. The way you are speaking uiungoganiza
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 21 день назад
longosola Fadah osawopa😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v 21 день назад
🔥🔥🔥
@RitaKainga
@RitaKainga 5 дней назад
Palibe Chinsinsi padziko lapansi, Mulungu amavumbulutsa zinsinsi zobisika angakhale pa nsi panyanja
@AngungaThatcherNgoma
@AngungaThatcherNgoma 21 день назад
Za boza izizi mumvere bho bho conversation yi. 😂
@BrownMainje-sh7hj
@BrownMainje-sh7hj 21 день назад
agalu kkkkk musiyeni president
@noahmshanga-rb1xc
@noahmshanga-rb1xc 21 день назад
Oh! No! This is serious.
@GwejeNundwe
@GwejeNundwe 21 день назад
Ngati ndimtukwane namachende ameneyu mxxx zaziiii
@Royhauya-uw2kr
@Royhauya-uw2kr 21 день назад
A government of national unity is possible but it will simply be to ransack the economy and go home.
@fidelixdezembro4599
@fidelixdezembro4599 21 день назад
Deus proverá
@HalistarStreet
@HalistarStreet 21 день назад
Nice greys❤
@Donvaga
@Donvaga 21 день назад
😂😂😂 hahaha km guys et
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 21 день назад
Mmmm lindani ofufuza .phuma bwanji?
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga 21 день назад
People of Malawi, greetings. How are you feeling? I know for most of you the pain of death is in your hearts, including Our President Dr Laz M Chakwela . Please let's take this time to unite and to console one another. Stop the blame game. It will not help us and our beautiful country. My fellow African brothers and sisters, I am also aMalawian citizen who loves his country deeply . Take the path of peace and stop destroying our beautiful country. The right honorable vice president will never return to earth. Just know that. Please honor his legacy by uniting your country. I am praying for the late vice president's family, our dear President and for the people of Malawi. Love is the way to go right now. I love you and will continue to pray for you . Williams Alex Mbonga
@AnastaziaMbewe-tj5md
@AnastaziaMbewe-tj5md 21 день назад
Sirent
@ChristinaChimombo
@ChristinaChimombo 21 день назад
Senseless
@user-us5hw4uy3t
@user-us5hw4uy3t 21 день назад
Iwe ndi kape fada wayaluka.
@WilliamKawaza
@WilliamKawaza 21 день назад
Akuyakhulayo ndindani kodi, sizochezeratu izi
@sylviachitseko397
@sylviachitseko397 21 день назад
Kodi can't we wait for investigation to finish first? Stop this please aaah
@LinessdorisScot
@LinessdorisScot 21 день назад
Mwamupha wapita basi,, kwasala muziphanano nokhanokha, ife as time goes tilimba mtima
@user-or7ng3fj8f
@user-or7ng3fj8f 21 день назад
Inu kodi mwadya chani kodi palibe chimene chikumveka apa 😢😢😢
@marypatriciamakuru226
@marypatriciamakuru226 21 день назад
Mwayaluka basi, mu Chikangawa munali Mulungu si mutiuza bodzaaaaaa
@laureenshaibu
@laureenshaibu 21 день назад
Voice of poor person iyi
@FelixMhango
@FelixMhango 21 день назад
Palibe funds yomveka apa timawona ngati muli ndi zinthu zogwilika. Komatu izi muzitenge bwino
@user-ox6rc2wn1p
@user-ox6rc2wn1p 21 день назад
Boza iwe
@ivymakiyi
@ivymakiyi 21 день назад
Umbuli at its best,,,,you want to hear what you think,,,,,,,
@YamzyAmos
@YamzyAmos 21 день назад
Koma 😂iweyo amene wapanga audio iyiyi anakupanga
@rholingssambale8274
@rholingssambale8274 21 день назад
Lankhulani chilankhulo choti muthe kukamba zomveka bambo. Nkhani yanu ndi yoti chani yomwe mwabweletsa???
@BensonChizenga
@BensonChizenga 21 день назад
😮
@user-tw9nl6ks9d
@user-tw9nl6ks9d 21 день назад
Mau a maluzi sasowa kmb edit yo mwaesesa ndithu
@MacBanda-df5zk
@MacBanda-df5zk 21 день назад
Kafukufuku ameneyo akhala opanda chilungamo ,this is Malawi ndikafukufuku uti unaphulapo kanthu kanzeru?wait and see.
@user-rz6xh8qg5r
@user-rz6xh8qg5r 21 день назад
Ndiye apa akuti bwanji. Kikikkkk
@PaulMalemba-pp8hk
@PaulMalemba-pp8hk 21 день назад
Foolishness at it's best. Tiyeni tikalime kuminda uku andale asiyeni sugar anapanga kale
@fidelixdezembro4599
@fidelixdezembro4599 21 день назад
Basitu apano zonse zaululika
@tendaimakamabviko5916
@tendaimakamabviko5916 21 день назад
Iwee wasowa zochita eti .....kagone !! Palibe chomwe chikumveka zomwe ukulankhula....ndiwe Cadet takudziwa iiiiiiya ....ungoti kukamba Ichi kusiya kukamba Ichi kusiya kagwere uko shatapu !!!!!
@FOSTERLUPIYA-zc1xv
@FOSTERLUPIYA-zc1xv 21 день назад
Pepani,God is with Malawi.U are trying to who?
@Christopher-xc2ey
@Christopher-xc2ey 21 день назад
Tayakhulani zomveka man mukuti chani kodi
@user-cj1nw7bi1k
@user-cj1nw7bi1k 21 день назад
Chitsilu cha munthu iwe ambuye akuone ndipo akuyendere ndithu
@LilyMbewe
@LilyMbewe День назад
Chidzungulilere 😅
@NellxXebo
@NellxXebo 21 день назад
Mulungu oziwa kuweluza akupaseni madaliso ochuluka .
@adamashrafi5875
@adamashrafi5875 21 день назад
Ukasuta uzingolima zitsiru inu
@SildaKatundu
@SildaKatundu 21 день назад
Kalikonse tikaona ,muyaluka
@SmartJumbe
@SmartJumbe 21 день назад
Machende tazirankhura zinthu zazeru Machende ako wanva ukumuyikira kumbuyo chakwera bwanji
@burtonjere-wn3qu
@burtonjere-wn3qu 21 день назад
Kodi ukuti chani iwenso ??? Tayankhula zonveka apa asah !! Ngat ulibe zonena osangokhala bwanji ..
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 21 день назад
Zimenezi sizinanveke?
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w 21 день назад
Waboza uyu
@usseintomasbacar8612
@usseintomasbacar8612 21 день назад
Munthuyutu sakuuza inu alipo amene amamuuza nde angotibenthulira
@alexanderntephea8706
@alexanderntephea8706 21 день назад
Chitsilu iwe iweyo ndi ndani? Watani Kodi? Sakunveka😮
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 21 день назад
Ife tikumva amene sanave zake zimenezo
@ReginaMhango-zn2iy
@ReginaMhango-zn2iy 21 день назад
Ayi tamva nawo zakuchipinda .. Ife tili chete kutchela nkhutu. Iponde fadaaaaa
@IssacMateyo
@IssacMateyo 21 день назад
Bodza lanulo mudzinama bwino big mani
@Lloyd-gd6pu
@Lloyd-gd6pu 21 день назад
Tadzingodyani gwada opanda tomatoyo inu
@user-ry9ql9jv3y
@user-ry9ql9jv3y 21 день назад
Bozailo mukulephera chizungu kikkk
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 21 день назад
Mcp khalidwe lonyasa sangasiye awa dzigawenga zawanthu izi Mulungu akukantheni nonse amene mwachotsa miyoyo yabale athu asanu ndi anayi
@knacktricky8521
@knacktricky8521 21 день назад
😅😅😅 bodza lakeso nde yayitu
@efkayshaun890
@efkayshaun890 21 день назад
😅😅palibe2 chmene chikuveka mwadya koma
@OFG-th3st
@OFG-th3st 21 день назад
😢😢😢😢
@andrewchiusiwa3487
@andrewchiusiwa3487 21 день назад
Musokosa chabe apa
@NEBERTMVULA
@NEBERTMVULA 21 день назад
CHAKWERA, KUNKUYU, ZIKHALE NG'OMA, CHIMWENDO BANDA, MKAKA, CATHERINE HARA be careful Malawians are watching. MCP HAS ENDED; IT WILL NEVER EVER BE AGAIN!!!!
@user-ru8xm6sk2n
@user-ru8xm6sk2n 21 день назад
Kkkkkkkk mangidwa nazo izi
@stevenghambi3471
@stevenghambi3471 21 день назад
Nde UTM mchita chiyani ndi chakwela???????
@SteveZale-pf1gk
@SteveZale-pf1gk 21 день назад
kkkkkkk agalu awa
@user-gh7zg5dd7l
@user-gh7zg5dd7l 21 день назад
Amwen ife sikut tili pano umawononga data ndi nkhan zake ngat izi plz ifa ndi ifa ndpo ikachitika imakhala kut yachitik basi
@noelchitimbe
@noelchitimbe 21 день назад
Kape iwe
@AllanaChiphazi
@AllanaChiphazi 21 день назад
Mwayambira pakati nkhaniyo bwanji?? Komanso Mulungu akuone ndi bodza lakolo and chilungamo akuchidziwa ndi Mulungu
@sokojane4015
@sokojane4015 21 день назад
Kkkkk zoyenda eshiii
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 21 день назад
Za ziii.mungoliubwa lubwatu apa
@khwimamtonga954
@khwimamtonga954 21 день назад
Chizungu chake
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no 21 день назад
Za ziiii kusowa zochita ,
@DivalaKaphaka
@DivalaKaphaka 2 дня назад
mcp nituvi malawi
@jackmuhura1797
@jackmuhura1797 21 день назад
Koma chizungu chavutapo apa
@marryphili5419
@marryphili5419 21 день назад
Koma ndiye zawo Zada basi panopa aliyese waziwa Kuti MCP ndi ya kumpha ndipo yizakhara history mupaka kalekale
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne 21 день назад
Achoke chakwera atinyasa kumpha vise wawo, nanga tikaasiya ampha angati.
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne 21 день назад
Enafe timadabwa anayàmba kumamupasa tima trip osaziwa amamuikira mbeza kuti akodwe, ngongore timabweza achakwera simukanawina zisankho panonkha popanda saulos ,,
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 21 день назад
😂😂😂 musamale kwambiri chifukwa ma activists amene alipo panopawa ndioopsa, ndima aliens so be careful you'll die without anything touching you
@greymitomoni4047
@greymitomoni4047 21 день назад
kwachema😆😆
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 21 день назад
Washoke chakwel please matogo yake
@user-ty4pq5ub3q
@user-ty4pq5ub3q 21 день назад
😂😂😂😂 Koma abale....
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 21 день назад
Mukufuna mudziwe mau ake eni eni kut mumuphenso wadya koma akuopa kufa mcp kkkkkk
@PatrickCk-wv2xq
@PatrickCk-wv2xq 21 день назад
Zautsiru izi umbuli
@amourvido8027
@amourvido8027 21 день назад
Za ziii ngat izi. Ma tittle kungoika just to attract anthu basi.
@VioletMaseko-ys4cu
@VioletMaseko-ys4cu 21 день назад
Koma bodza lakelo😊
@jomochirwa
@jomochirwa 21 день назад
Koma bodza ili simudalikonze bwino tsopano mwayamba kunyozetsa za chisonizi.wosamatelo ife tili ndi chisoni esh.
@user-lb8xz9lt3z
@user-lb8xz9lt3z 21 день назад
Kodi wamwa ambuye ntengeni akuyankhula apayutu
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 21 день назад
Mudziona simunati aphwanga mfiti Inu akapolo inu
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 21 день назад
MCP ndiyoipa kwambiri
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 21 день назад
Osamaoneka kuchenjera pa gulu dekhani
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 21 день назад
Zaziii kodi mukumsowa nkhani yoti mutchukire pano???
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p 21 день назад
Kodi awawa akuti bwanji nawoso awa,,English yikunvuta ndiye akulankhula ngati amalankhulana ndi mabwana😂😂😂koma 😅😅😅😅kodi mukufuna mutchukilepo apa eti tamakangokumbani mbewa uko basi
Далее
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 157 тыс.
🤯 #funny
00:20
Просмотров 1,7 млн