Тёмный

ACB LAPEZA KUTI BOMA LA MCP MWACHULUKA KATANGALE 🙌🙌🙌 

HOT 265
Подписаться 63 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

3 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 45   
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 дня назад
Vuto la boma ili ndiloti, onse, maka MCP representatives, anali amphawi okha okha. Nkani pano Ali pa phwando la a kakowa
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 дня назад
Kodi Ku Malawi kuli Anthu oona patali ngat inuuuu...for sure its true
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 дня назад
Corruption can say goodbye if only the Anti corruption bureau becomes non governmental organization
@RodgerChaula
@RodgerChaula 3 дня назад
Our Gorverment is lotain Asogoleli .anthu awa alibe umunthu othandiza ziko lawo
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 дня назад
Ine ndikugwirizana zawo abambo ayambawo kuti bungweli lithe basi, likungowononga ndalama za boma.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 дня назад
Koma Chakwera ndi achina Chimwendo Banda akuti boma likuyenda bwino kwambiri. Eeeeeeeee! Anthu awa sadabwere kuthandiza dziko, koma kudzadya. It's a shame. Achoke basi
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 3 дня назад
Bakili mluzi TV adanena kale kuti MPC yasakaza koposa😂
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 2 дня назад
Inu ana amahule adana naye bwanji katangale mesa bambo ao analowa kwa mao mwachinyengo😂
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 дня назад
Katangale atha kuthesedwa ngati atsogoleri ndioopa Mulungu moonadi munthu wopana kuopa Mulungu angapange bwanji chilungamo.ziko la Malawi likusowekera atsogoleri achilungamo. Chawiri ACB isakhale yisalamulidwa ndi boma. Chachitatu kumalawi tinakula kuti ukalemera anthu azikupasa ulemu ndichimene atsogoleri akuba ndalama akufuna ulemu
@mussamapira801
@mussamapira801 День назад
Bwezi akulandidwa katundu ndi ndalama zomwe akubawa bwezi kubaku kutatha koma from 1964 up to now palibe ndi modzi yemwe adalandidwapo katundu ndiye chifukwa chake kubaku zikukutha kumawalanda katundu ndi ndalama zomwe basi
@mathewsnachuma8086
@mathewsnachuma8086 3 дня назад
Anthu onsewa adali osauka that's why
@user-ni4ri2xe9e
@user-ni4ri2xe9e 2 дня назад
kumudzi kwathu kuno ku Malawi ndimadabwa kuti kodi bungwe limeneli la ACB likutani komanso why do we say that we have ACB yet corruption instead of coming down komano ili pa makwerelo kupita mmmwamba. mwachitsanzo passport ya MK50,000 kuti ifike mmanja mwa M'Malawi nde kuti akhala atagwiritsa ntchito makobiri opyola mk200,000. ngati otsogolera ali serious to deal with this nde kuti all juniors will be afraid. ndizovuta kuti katangale athe ngati otsogolera akupanga nawo.
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 3 дня назад
ndi boma la mbava zokha zokha zakatangale ndi kupha chakwera ndi chigawenga cha kuba ndi kupha
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f 19 часов назад
ACB yili ngati nthambi yoyima payonkha koma boma Lili NDI mphamvu kuwophyeza kuti milandu yisapite KU court. Waste of money KU ACB
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 2 дня назад
Kodi kumalawi kuliso boma inesindikuona boma soapa ndikuona mbava
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 3 дня назад
Ayi osati osaukafe koma umakhala munthu utatopa ndikuyemdera that is why umangopeleka ka deal kkkkkk koma zoona chakwera mmmm
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 3 дня назад
Mtsogoleri sayenera kuyang'ana nkhani yakatangale ndi nkhope yachisomo ayi. Apa pokha akuyenera atchedwe kuti dictator pofuna kupereka mantha kwa onse oganizira zokachita mnchitidweu. ACB payokha singakwanitse. Komanso katundu ndi ndalama zidzibwezedwa ku thumba la boma, kuti zitumikire moyenera.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 дня назад
Moti kuti munthu awadzudzule akum'manga, what type of government is this.
@SamJalie
@SamJalie 2 дня назад
Evil government full of intimidation and hypocrisy
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z День назад
Mmmm mm koma kumalawimu
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 3 дня назад
I wish it's high time boma limayenera kuganizira zosintha malamulo athu okhuzana ndizakatangale ndikuika zilango zokhwima osakhala izi zomangoti basi abwenza ndalama ndiye takhululikira kapena akamangidwa kungokakhala Chaka chimodzi kenako aziti amachita behave bwino ndiye boma lawakhululukira, mmene tikupangira ndimilandu yogwililira kapena murder zomwe zomwezo zitabwera kukatangaleku, munthu azikakhala even 9 years alipa alimand anthu tiziopa kugwira chaboma,panopo chinthu chomwe chikutisaukitsa amalawi ochuluka ndikatqngaleyu,ine ndimaona kuti mmene tinathana ndiulamuliro wankhanza wachipani chimodzi wa MCP ndimaona ngati pamafunika pabwere Chihana kapena Muluzi wina yemwe angatimasule kusinga zomwe zatimanga kukatangale
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 дня назад
Nthata za njala izi ndipo mistake yomwe tinapanga a malawi mulungu atikhululukire ndithu...
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 дня назад
Ngati anabisa black box kulibwanji report ya Chilima?
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 2 дня назад
Ndimbamva zokha zokha zimenezo mcp anthu onse anali alimi ndie atani anthuwo akhala ali pa ulimi kwa zaka za mbili ndie asabe Mesa khotse mu mteza simukuona pamenepo kuti mbuzi aimangilila pa mbale ndie mumati ingatani Mesa kungodya mbaleyo mowonongaso ka kuti mwai umenewu suuzapezekaso ka 😂😂😂😂
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 2 дня назад
Katangale sangathe chifukwa ose ali m'boma akuba
@SamJalie
@SamJalie 2 дня назад
Kupeza apeza nanga akupangapo chiyani pofuna kuthana ndi katangale?
@JuuuKomba
@JuuuKomba 2 дня назад
Katangale kuthi athe ndi mopweka vuto mukumasakaniza ndi school opezeka wapanga katangale asamangidwe koma amenyedwe paulu kumumangilila pa bwalo athu akuona athu atha kusiya
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 3 дня назад
Chakwela you mast go
@bornface4786
@bornface4786 2 дня назад
Katenga okhoza kutha ndinthu komano anthu akupanga dala chifukwa choti malamulo anthu Ali so week let's we say titati tipange lamulo loti aliyense ogwira ntchito m,boma akapezeka ndi mulandu wakatangale azipatsidwa ban kuti sazagwiranso ntchito m,boma mpaka kalekale. Ndithu vuto limeneli likhoza kutha ndithu
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw День назад
Basi tu kusazikana kumeneku achakwera muusiya mpando bola tiwone amanganya wo
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 2 дня назад
Pakufunika kusintha malamuro ena ya dziko lino, munthu akapezeka ndkatangale anyongedwe bas mzaona kuti katangale wayamba kusika chifukwa anthu azawopa kufa, komaso acb ithesedwe chifukwa palibe chimene ikuchita.
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f 19 часов назад
ACB is useless Atsogoleri kuyambira 1994 akhala akuba ndalama koma milandu yawo siyithera Kuma khoti. Ndiye justice system NDI useless chifukwa amavomera kutseka milandu popanda chigamu
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 2 дня назад
Cover the boss
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p 2 дня назад
Chakwera must go
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 2 дня назад
Ife izizi tatopa nazo ameyo achoke basi. Chifukwa mmutu mwake mwadzadza mamina.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 3 дня назад
So sad💔💔
@user-xs3pk1vp8i
@user-xs3pk1vp8i 2 дня назад
Mabodza okhaokha
@PatrickMulangala-os4by
@PatrickMulangala-os4by 2 дня назад
Achoke
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 2 дня назад
katangale m'malawi mkovuta kutha chifukwa president ndi nduna amapatsidwa mphavu zambiri so mkovuta kut zinthu zina zikomzeke m'malawi muno
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 3 дня назад
Pali boma limene lingabwere lopanda katangale palibe chachilendo zidalipo kaleso
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 2 дня назад
Bwana apa zawonjedza koma inu muli dziko liti....tatiyeni. Tizimvako chisoni plz plz
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 дня назад
@@GospelSoldiers-sr7np mpata ulipo ositha boma koma musaganize kuti mavuto amene alipowo angathe
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z День назад
Tingovomela mavuto kumalawi
Далее
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
Просмотров 1,3 тыс.
Luiza Rasulova #luizarasulova
00:37
Просмотров 613 тыс.
Сумерки сасага🧛
11:41
Просмотров 1,2 млн
MZIMU WA (SOJA LUCIUS BANDA)UUSE MU NTENDELE
1:45:51
Просмотров 6 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Nthanyulingz
14:18
Просмотров 6 тыс.
ZAYAMBIKA TSOPANO/ TIONA ZINTHU CHAKA CHINO.
19:02
Просмотров 7 тыс.
DPP Chiradzulu today
3:03
Просмотров 1,8 тыс.
kumalawi kuno ndani wandale angamake??
1:01:32
Просмотров 4,7 тыс.
Luiza Rasulova #luizarasulova
00:37
Просмотров 613 тыс.