Тёмный

Achakwera Sakupanga Zinthu Mmene Adalonjezera | Wina Wazuzula Mmene Zinthu Zikukhalira 

Mukuziwa?
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

#chakwera #chilima #malawi #trending #news

Опубликовано:

 

27 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 60   
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo Месяц назад
Mwayakhura bwino kwambiri ❤ ndipo athu awa achoke mwankhaza mademo achitike ife tikumva kuwawa amalawi
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z Месяц назад
NO PAIN NO GAIN TIYEN PASEO ON 10 JULY BASI CHAKWELA ACHOKWE BAS WALEPEL NO PAIN NO GAIN
@JustinLipipa
@JustinLipipa Месяц назад
Afiti awa a Congress, Congress singasinthe ndi ng'ona zokhazokha izi aaaaaa
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Месяц назад
Ndipo zachita kuonetseratu kuti ngozi yandege imeneyi anachita kukoza zimenezi imene taluza abale athu 9 imfa yamamgawa simasowa ayi Lazaro ndi anthu ake ndi dzigawenga
@user-rm2xv8ys1i
@user-rm2xv8ys1i Месяц назад
Vilombo ivi
@HamidaIweni
@HamidaIweni Месяц назад
Mwandiyankhula bwino kwambili❤
@TamalaSoko-vg5wq
@TamalaSoko-vg5wq Месяц назад
Munena zoona brother ambuye akudalitsen
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 Месяц назад
Your speech is good bro, keep it up
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Месяц назад
Tilankhulireni anzathu inu ife atitseka pakamwa akuti tisamalankhule Mau anphanvu amene mwanena ndithu ambuye akudalitseni Ifeyo nde tikulira misozi yathu sidzatha 😢😢😢
@MphatsoChengetani
@MphatsoChengetani Месяц назад
Very good speech
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 Месяц назад
Kulankhura mwa nzeru uku koma oipa adana nazo.Wandale amafuna atakhala zaka zochuluka paudindo yet akapeza mwai mmalo mogwira ntchito to gain trust kwa anthu onse amakhara busy ndi 'kwapsya tonola' mkumaembekezera kuti akaba ndalama ,ndalama zomwezo azapangira campaign kuti awine.Chitani zinthu zabwino kuti zabwinozo zizakupangireni campaign zokha popanda kuononga ndalama zanu Mwai munapatsidwa ,mukuutaya nokha
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z Месяц назад
Poor people feel the pain right now
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 Месяц назад
Ndi agalu awa brother palibe zonse analonjeza zaboza zonkhazonkha chilibe zeru iiiiichiiiii
@user-be3is8rc4r
@user-be3is8rc4r Месяц назад
Good speech
@TadalaPaul
@TadalaPaul Месяц назад
Umumu muli mfundo guyz i proud for you vp
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Месяц назад
Mmmh pali anthu amene anapatsidwa luso lolankhula ndithu nkulu uyu akulankhula momveka ndipo ndutha kuona kuti ndithu dzikoli panalibe chifukwa chobwezeletsa anthu opandanzeruwa , Nkulu iwe mulungu azikuteteza komanso mukhale healthy
@PetroMatias
@PetroMatias Месяц назад
👍👍👍👍👍👍👍gud
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x Месяц назад
Security departments kusanduka ya a chakwera aaaa zokhumudwitsa kwambiri 💔 God knows everything.🙏
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
4:10 4:10 4:10 4:11 4:11 4:12 4:12 4:12 4:12 4:12 4:13
@yohanezimba8329
@yohanezimba8329 Месяц назад
The problem is Malawians make decision during anger, and 2025 will do the same similar choice because of anger. Others they are speaking as if they are wise but the true sense these people if they happen to be chosen they will also worsen this country
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r Месяц назад
Exactly the point
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 Месяц назад
This guy is saying zoona, just imagine celebration ya ku sankhidwa kwa Mr Usi ngati VP? Shame shame
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke Месяц назад
Chipani ichi 🙌🙌 ndimkangomva ine
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z Месяц назад
Ineso eeh
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r Месяц назад
Vc president ameneyo ngamene agulitsa Chilima amene amakonza zothetsa Tonse Aliance. Iye, pamwambo anati; Chakwera ndi wake komanso Chilima ndi wake. Kodi pamene amanena izi, Chilima ali kuti?
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE Месяц назад
Alibe nzeru awa
@hussenadam3786
@hussenadam3786 Месяц назад
True Malawian
@FrankAdonis-zl6qc
@FrankAdonis-zl6qc Месяц назад
Ulamuliro upusa even mwana wachichepele sangaganize mopusa ngati chakwerayu
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt Месяц назад
Adafa pa mdipiti wopelekeza maliro aja samalawi? Kodi Malawi ndi anthu amayina okha?
@FrankAdonis-zl6qc
@FrankAdonis-zl6qc Месяц назад
Chakwera achina zikhale ng'oma and other team opusa zitsiru za anthu oma ankhula America English koma athu opusa ngati nsima
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op Месяц назад
Kuyakhula kwa bwino
@GrolyGondwe-e9s
@GrolyGondwe-e9s Месяц назад
Zilombo zimenezo
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Месяц назад
Muone ma tie amene ali pakhosi atau afira magazi okhaokha. Onani chithunzi chili pa video imeneyi.
@user-um6ob9sf3g
@user-um6ob9sf3g Месяц назад
Achakwera ndi gulu ace wakanika
@Uncle_B265
@Uncle_B265 Месяц назад
Malawi tinagulisa uyuu
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Месяц назад
Namu bwana mukuyangu rabwinino man big
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
Chakwera sangarire ayi chifukwa iye.niamene.wapha.chirima kkkkkkkk mubusa kumuchosa ku mzuzu.kukamusiya.ku lirongwe amafuna kuti akamuphe.ndipo akamudwe ku nyanja kuribe magazi ndeno amafuna magazi kkkkkkkk koma chakwera sataniki
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Месяц назад
Akulephera kumanga kumkuyu okupha Allan witika koma kulimbana ndi bon kalindo mcp ndi ya satanic
@WisdomBlack-uu7zt
@WisdomBlack-uu7zt Месяц назад
Za kugwa kwa ndege akudziwapo kathu awa ndichifukwa bwana aja anauzidwa kut ndege malo
@KhalideNerve-mu1eq
@KhalideNerve-mu1eq Месяц назад
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@EssaPindani
@EssaPindani Месяц назад
Koma walephel kuyendesa malawi unku uyu achoke
@DavieChiwale
@DavieChiwale Месяц назад
Sitikusowanso zabwino kwa afiti amenewanso atsala ndi masiku owerengeka
@AllanChabwela
@AllanChabwela Месяц назад
Mukuyankhuladi chilungamo zaonjeza
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Месяц назад
Munthu asanafe mumayamba kugontha nimukhutu
@ziyamikanmakowa5981
@ziyamikanmakowa5981 Месяц назад
Mfiti za anthu izi
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 Месяц назад
Zowona alimife tili mumavuto
@leviefeston7626
@leviefeston7626 Месяц назад
Apolice ndi opusa kwambili Amalavula chingamu ndi mtegmdza olawa MCP ichike
@user-xe1so5xj2w
@user-xe1so5xj2w Месяц назад
Chakwera andipatse vote langa ninalakwitsa kuwavotere
@raphaelfanuel4608
@raphaelfanuel4608 Месяц назад
Inu simunalemekeze maliro asanachitike bwqnjiii
@AckimMhango-v1x
@AckimMhango-v1x Месяц назад
You are talking
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Месяц назад
A nkava kuwawa mu mtima ankangonena zimenezo koma sakugona asiyeni azuze anthu tsika mu mtengomo a tipeza a Malawi pansi pano
@MisheckAselo
@MisheckAselo Месяц назад
Yonseyi ndi mission ya chakwera, koma iye akutsogoza anzake iye azamka kuti sikumanda basi a chakwera be careful pple we watching you 🖕
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Месяц назад
Tiyeni Amalawi tigwilizane anthu awa achoke basi
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON 25 дней назад
Mpaka muyaya kuti dzikoli adza nkhare ndi family yakwawo lokha tuuuuu amenewa afika poti akhoza kuthila poison mmadzi kuti athu onse afe pamene zafikiramu chifukwa tuuuu apapa chimbare chakalika
@FrankAdonis-zl6qc
@FrankAdonis-zl6qc Месяц назад
Democracy will never demolishe we are in new generation
@MandalaChaona
@MandalaChaona Месяц назад
Evil men,Greedy, Jealousy men. Wait for your judgement day. Mulingati abwino popeza nyansi zanu zabisika
@user-wb9ji3oe5o
@user-wb9ji3oe5o Месяц назад
Yankhulani tikumveni
@chachaamoah3592
@chachaamoah3592 Месяц назад
Wa MCP sasowa uyu.mulibe nzeru MCP boma lazitsiru
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z Месяц назад
Machende ako
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
4:10 4:10 4:10 4:11 4:11 4:12 4:12 4:12 4:12 4:12 4:13
Далее
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 50 тыс.
Это реально работает?!
00:33
Просмотров 4 млн
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Просмотров 138 тыс.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 111 тыс.
Interview ndi Norman Chisale
1:05:22
Просмотров 231 тыс.