Тёмный

Bon Kalindo lero pa 11 July kufotokoza mopanda kuopa aliyense - “MUNDIMVA NDIPO SINATI” 

Makosana
Подписаться 65 тыс.
Просмотров 31 тыс.
0% 0

Опубликовано:

 

9 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 81   
@user-ix2ux5ss1b
@user-ix2ux5ss1b 20 дней назад
More fire mukutiimilira bwana! Ife timasowa mpata oyankhura zakukhosi kwathu. God bless you and protect you. Amalawi tikuvutika
@EversDman
@EversDman 18 дней назад
Bon kalindo wathu wathu 🔥🔥🔥💯
@PeterKasiya
@PeterKasiya 19 дней назад
Boniiiiiiiii kalindoooooooooo Mwana owopswa kwambili
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji 20 дней назад
Mukazava kuti boma lawanyera ndi zimenezo anavako kuti Koma Malawi ayi ndithu komaso kamuzu samapaga zimenezo ayi amati zithu zikamakwela iyeyo amakambolana ndi anuwake kamphani kuti atsitseko anthu ake alibe ndalama ndiye inu mukuzitega bwanji zimenezo kodi dziko la Malawi mwalitani tamakumbukirani komwe munali azanufeso tikuva kuwawa ngati munkhavera inu muja kuli mulungu kumwamba zonse mukupagazo akuziwona ndithu tsiku lina lidzakwana la 40👏👏
@LuyoloTlhapane
@LuyoloTlhapane 13 дней назад
A pule athu ❤❤❤god protect your mr born mmatiimilila
@MomeryPhiri
@MomeryPhiri 19 дней назад
❤❤❤❤❤❤❤ love it
@user-kk4uj8ko8k
@user-kk4uj8ko8k 20 дней назад
bon kalindo sukunama luchenza. Lijoni ikupanga khazakwambili longopackngi 1ooooo u lube amakumanga kuselo
@user-xm5cq1fb8g
@user-xm5cq1fb8g 19 дней назад
Ulemu wanu big❤❤❤❤❤
@DauglassNkhoma-dj9lp
@DauglassNkhoma-dj9lp 19 дней назад
😂😂Boni kalindo wangadula kkkkk boooo towopa kubwelako kumalawi
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 19 дней назад
Kkkk koma abare zowona mchenga omwewo omwe analenga Mulungu mwini nthaka zowona mpaka kumagulitsa ayi zikomo dziko ili 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
@user-dj6rc3lc4t
@user-dj6rc3lc4t 19 дней назад
Inu ndinu Muthu wankulu kalindo Bon mumakwana
@FarookRaphael
@FarookRaphael 19 дней назад
More fire komanso mukuyankhula ngat chinyanja service channel Africa
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem 20 дней назад
Big up bro
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 19 дней назад
Ndipangeso replay pakanyimboko kandisangalasa bwanji kkkk koma uyu ndi pangolin 😂😂😂😂😂😂
@FlorryVugy
@FlorryVugy 19 дней назад
A president Bon mumatiyimilira😂😂😂😂😂 Sikusinja ndi gwenembe😂😂😂😂
@UthmanKapungu
@UthmanKapungu 20 дней назад
Fire!!!!!!!!!! Bon kalindo nazoni tatopa ife
@AffickChaona
@AffickChaona 16 дней назад
❤❤❤❤❤
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j 19 дней назад
Aaaaa yai awawa akufuna kuti tiyiwale kunlankhula za chilima. Agalu a anthu ndithu
@user-lg6ym4hz3w
@user-lg6ym4hz3w 20 дней назад
Kkkkkkkkkk ana ofewa odya mipungu nthawi ya mayeso apolice akungosilira
@EllinaBitto
@EllinaBitto 19 дней назад
Bulaza wathu❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@NdawaPhillipfortunePhakatie
@NdawaPhillipfortunePhakatie 19 дней назад
Motor 💥 kalindoooo
@user-wm4rs4kd7d
@user-wm4rs4kd7d 20 дней назад
@user-zt3gv7md6x
@user-zt3gv7md6x 18 дней назад
Zoona amwene
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 20 дней назад
😂😂😂😂😂 lero wayaka moto kalindo❤❤❤❤❤ a opposition please chitanipo kanthu awawa aikanika dziko olo manyazi alibe
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 19 дней назад
Awa ndi machine poyankhula the DC mwana wowopsya kwambiri 😂😂😂
@nicholasmutano6017
@nicholasmutano6017 20 дней назад
Uyuyu ndi mandrax sichamba, akufuna titani tilowele kuti si misala iyi?
@PeterMaulana-qk5uq
@PeterMaulana-qk5uq 20 дней назад
Ooh...ambuye dalisani anthu amene akumenyela ufulu m'malawi chonde musalore kt mbava za mcp zilamulire dziko lathuli AMen!!
@FwasanMwenefumbo-zq7sg
@FwasanMwenefumbo-zq7sg 20 дней назад
The DC 🔥
@BernadettaTengula
@BernadettaTengula 19 дней назад
Koma ine uyu ndimasowa pomuyika ,,ati chifukwa cha udindo😂😂😂
@ericlarks8165
@ericlarks8165 19 дней назад
,🔥🔥🔥🔥
@JoyceChitsulo-mw7wg
@JoyceChitsulo-mw7wg 19 дней назад
Makosana apa nde mwapita
@FrankMilias-og3js
@FrankMilias-og3js 19 дней назад
Kulankhula mosaopa nyooo sss winiko
@user-hq8fw5hz2l
@user-hq8fw5hz2l 19 дней назад
Awa ndie mawu
@user-dm6xq6cp1m
@user-dm6xq6cp1m 19 дней назад
Ai zikomo 🥱
@HelenamoisésLisboaMoisésLisboa
@HelenamoisésLisboaMoisésLisboa 20 дней назад
Ambuye akudalitsen
@benjulius6070
@benjulius6070 19 дней назад
😂😂😂😂😂😂
@gerrardgladstone2473
@gerrardgladstone2473 19 дней назад
Akuti kufuna kumangidwaaaaa 🤣🤣🤣
@EdwardMukholi
@EdwardMukholi 20 дней назад
Kkkkkkkkkk koma chakwera ndiye ndiye zikuchoka kuti zimenezi
@ChisomoamitoniSauzandeamiton
@ChisomoamitoniSauzandeamiton 19 дней назад
bwana ng'alurani ndithu tili nanu nanu
@SmartMoles
@SmartMoles 19 дней назад
Zofunikila kulangura mwayangure kumene
@VincentMalika-w7x
@VincentMalika-w7x 20 дней назад
Ndipo eeeeee tikudziwona kuno tikulemba mayeso apolici ache akupemphaso dzokudza zakudya zath
@directorkfuture118
@directorkfuture118 19 дней назад
Ameneyo asamwe mowa 😂😂😂
@user-tw5iw7gf2v
@user-tw5iw7gf2v 19 дней назад
😂😂😂😂 mpaka muchenga license
@RamseyWasi
@RamseyWasi 20 дней назад
Blasa, Malawi saadzatheka mpaka kale kale. This is my second SMS to you mr Dangerous Child (DC) My opinion: Kungosiiya utsogoleri wa anthu osawukawu.chfkwa or titatan,kusawukaako sikudzaatha.
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 19 дней назад
Aliyese ndi wakuba koma kusagwidwa Judgement day tidikire oweruza
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 19 дней назад
Ubwino wake ukuzimenyera wekha khondo uzalemera wekha
@user-kx4cj7iu9q
@user-kx4cj7iu9q 19 дней назад
Dc
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 19 дней назад
Mpakana tizigulisana mchenga wamudziko lathu zoona?, kusavukatu uku sopano aati!?, chaza ndiyan choti tizikhala ndi linces yovuwulila mchenga ?, ndepoti amalawi mumkafuna kusintha zinthu , zimene mumkafuna kwa abusa zija mzimenezi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤ , mo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mcp kkkkkk
@HendersonDziwa
@HendersonDziwa 19 дней назад
Dzelu zachepa kkkk
@DaudiAbdullah-o5l
@DaudiAbdullah-o5l 19 дней назад
Mumatiyimilila
@TshepoModise-xs4qu
@TshepoModise-xs4qu 20 дней назад
Koma nkhaza zake mpaka licence ya mnchenga Mmmm zovuta bwanji eeee
@maxwellcaptain3937
@maxwellcaptain3937 20 дней назад
Kalindo samaopa😂😂
@PeterGrant-ih1sr
@PeterGrant-ih1sr 19 дней назад
Athuawa atakhala alipo okwana 4 ziko muno athuwa atasitha ndithu😂😂😂😂
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 19 дней назад
😂😂😂😂😂 koma DC
@D.RJALLI-qo6yd
@D.RJALLI-qo6yd 19 дней назад
Ine ndikudana ndi ma opposition akumalawi ndi agalu kobasi makamaka dpp ikungoyang'anila wosalangula khatu kumbonà lamasuso ngati ili ndiye boma adzalipesa bwanji dpp tadzukani ife tampudzilapo ndipo talapa mamisiteki athu bwelani nditu mutiwombole kwa agalu awa
@MathpeterLemon-ls1ns
@MathpeterLemon-ls1ns 19 дней назад
Ati kutitola kapena chani
@JuliusMunthali-z7j
@JuliusMunthali-z7j 20 дней назад
Awuzeni
@ChrispinEdward
@ChrispinEdward 19 дней назад
Bwanawe pafika boma umuthu walimbe akungo funa kumupanikiza Muthu osawuka kut azikhala ndima strees bas komano azidikile kut Pali mwambi waphala lakaka ukaza fika pomva kukoma limakhakut lathamo mupoto
@user-ls5zj8qn6k
@user-ls5zj8qn6k 20 дней назад
Koma uyu inu kkkk ati apolice osilila mpunga wa nyama 😂😂😂😂 ayi zikomo
@AnthoniohMazengera
@AnthoniohMazengera 18 дней назад
Hahahahahahahahahaha😂😂😂
@Aluwenkareem-ev3ro
@Aluwenkareem-ev3ro 19 дней назад
😂🤣😂🤣
@lytonmaseko4534
@lytonmaseko4534 19 дней назад
😂😂 kung'alulatu
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 16 дней назад
😂😂😂😂msusi olo nthuli amatayapotu a dpp
@GiftKulture
@GiftKulture 19 дней назад
🤣🤣🤣🤣 mipunga
@AaronLitete
@AaronLitete 19 дней назад
Kkkkk boma lopusa
@YonaMartin-kb3do
@YonaMartin-kb3do 19 дней назад
😂😂😂😂 akavoterana ndi amawo yemweyo kupuma palibe
@user-yl3lg5fk8f
@user-yl3lg5fk8f 19 дней назад
Koma amalawi tinalakwanji kt tizunzike,,,galu uyu wazunza miyoyo ya anthu osalakwa,,chitsiru cha m'busa munthu opanda conscious
@sir-wanton-2001
@sir-wanton-2001 20 дней назад
Kkkkk Kkkkk uyu akazankhala president azamujaje nda uyu ndi dolo
@ikmusic-s9f
@ikmusic-s9f 20 дней назад
koma nde eeee mpaka licence mchenga
@YohaneMbewe-u4k
@YohaneMbewe-u4k 19 дней назад
😂😂😂😂
@user-ky8us1ff5b
@user-ky8us1ff5b 20 дней назад
😅😅😅😅
@wangachindeya8577
@wangachindeya8577 20 дней назад
Bigiliman naweni
@user-vn1wq6wg6i
@user-vn1wq6wg6i 20 дней назад
K.K😂
@PhillipMtonga-g7o
@PhillipMtonga-g7o 20 дней назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 zamanyazi kuntonse alliance
@BenjaminKayembe-j7j
@BenjaminKayembe-j7j 20 дней назад
km eeee awawa ndsbwsna gayz mmmmmm amakwana km
@Kachelephiri
@Kachelephiri 19 дней назад
Awa.akulila.ayesetse.2025.azawinekwawo.ump.kwawo.kma.ngatiakukanakwawo.ndiakanene.jilose.tingamuvele.galu.wachabechabe.
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 19 дней назад
Uku nyoza bon kalindo,, zeru ulibe iwe uku Kanika kulemba kumene galu iwe
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 19 дней назад
Yamba wapita Kaye Ku school ya mkaka uziwe kulemba...... galu iwe
@user-wz6jy3re8n
@user-wz6jy3re8n 20 дней назад
😂😂😂😂😂😂
@MadalitsoManyozo
@MadalitsoManyozo 19 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂
@myheartforkids2876
@myheartforkids2876 20 дней назад
😂😂😂😂😂
Далее
A Michael Usi Inu Si A UTM - Lyton Mangochi
23:13
Просмотров 6 тыс.
КАК Я ЭТО СДЕЛАЛА?
00:13
Просмотров 138 тыс.
Документы для озокомления😂
00:24
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Просмотров 48 тыс.
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
КАК Я ЭТО СДЕЛАЛА?
00:13
Просмотров 138 тыс.