Тёмный

BON KALINDO LERO PA 6 JULY 2024 | 

DZIWE TV
Подписаться 22 тыс.
Просмотров 33 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

4 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 133   
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 11 дней назад
Kungotipela Born Kalindo achakwera sazagona ku state house 😮😮 ndipo malawi wina aliyeze sazagona izi nde mudziwe achakwera 😊😊😊
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 11 дней назад
Bonnnnn Kalindooooo the DC chimwana cholimba mtimaaaaaa😅😅 love you more!
@user-fg8qy7jb2q
@user-fg8qy7jb2q 10 дней назад
Kuyakhula chilúngamo Bon akuigwira ntchito more than zipani zotsusazi. Big up Bon, kaya anthu anve or asanve better wayakhula💪💪
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f 11 дней назад
Komatu the DC amalangiza Chilima Ali moyo kuti atuluke mu tonse then Chilima ananyalanyaza mapeto ake anaphedwa.
@spargomw
@spargomw 11 дней назад
Mtsinje wa timkanena udathera mu siizi😢😢😢
@MatressKanyenga-f1z
@MatressKanyenga-f1z 11 дней назад
🔥 kulavula moto big boss kalindo ❤fire 🔥
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 11 дней назад
We love you Mr president you fight for us poor people
@AndrewBurton-iv2zm
@AndrewBurton-iv2zm 11 дней назад
Brave man we're very appreciated
@MosesKalenge
@MosesKalenge 11 дней назад
Good news mr brother ♥️♥️♥️♥️ bon kalindo 💪💪💪💪💪💪💪✊✊✊✊✊✊✊
@GeorgeChikwatu
@GeorgeChikwatu 11 дней назад
Kkk achikulile olimba mtima
@SphiweBwanali
@SphiweBwanali 11 дней назад
Mumatiyimirira akalindo God bless kalindo❤
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 11 дней назад
dziko la Malawi likukhala ngat nyanja yoti aliyese akhoza kusambiramo ndi kutuluka. anthu ali m'boma nsaname akusambira paliponse
@fracsonNanjala
@fracsonNanjala 11 дней назад
Zomadinda ma stikcer pa boder zija zathanso 😅 more fire boni kalindo
@PatrickMailos
@PatrickMailos 11 дней назад
Booooooooooon kalindo 💪💪🔥🔥🔥🔥🔥
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 11 дней назад
Kalindo his DC indeed akupanga masewera aboma
@nonhlanhlanhlanhlo3907
@nonhlanhlanhlanhlo3907 11 дней назад
Ulemu wanu mr Dc timenyeleni nkhondo basi mwina ifeso tsiku lina tizakamba zokoma tikudya katatu patsiku
@JimmyPindani-pu4ez
@JimmyPindani-pu4ez 11 дней назад
Mumakhwana munthu wamkulu🎉🎉🎉🎉
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 11 дней назад
Maina wo muwawulure bas DC akamuna fire on duty keep it up
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 11 дней назад
The DC ❤❤❤❤❤ Koma uyundye mamuna eeeeee
@FrankWaresi
@FrankWaresi 11 дней назад
Bwanawathu wathu the DC chimwana Chopanda matha❤❤❤❤❤❤
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 11 дней назад
Namu Dc ❤❤❤❤ wi love to ❤ kuswa kuswa basi chakwera machende ake
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo 11 дней назад
Ndizamanyid zimenezo iyya
@KennethFedison
@KennethFedison 11 дней назад
Bon kalidoo sakunama tilikoko,🔥🔥🔥
@UTHMAN-WAYA
@UTHMAN-WAYA 11 дней назад
Wise man the DC❤
@TimothyKabumbuKendrix
@TimothyKabumbuKendrix 11 дней назад
We absolutely appreciate the DC, THE DANGEROUS PERSON.
@user-dh4xl3jb9d
@user-dh4xl3jb9d 11 дней назад
Boooooooon kalindooooooo the DC mumatiimilila mulungu azikutetezani
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 11 дней назад
Zoonadiitu Mr bon kalindo bomaili ndi lamanyi lauchitsilu zikuchitikazi ndi za manyikobasi
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 11 дней назад
Kuno Kumalawi Tendendele tilibe dzimakhala zonvesa chison ponva kuti ndife anthu opemphera koma tili chabe
@hassanhassyduwa3212
@hassanhassyduwa3212 11 дней назад
More 🔥 📛 🔥 fire
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 11 дней назад
Kikikikiki, chipangolini sopano. Auze amazolowela agalu amenewa.
@IdahChristopher
@IdahChristopher 11 дней назад
The last man standing 🔥🔥🔥
@ErnestChansa
@ErnestChansa 11 дней назад
Mr president anthu awuphawi palibwino ayimile u president waziko pasogolopa tizawona kusitha ulemu Mr president born kalindo chonena chimandisow mulungu azikudalisani thawi zose
@JohnKandodo-mb9rx
@JohnKandodo-mb9rx 11 дней назад
Za power Mr kalindo
@WestonGawaza
@WestonGawaza 11 дней назад
Akunena zowona akalindo ziko silikuyenda abakili ana pangapo border free anali ndindalama anthu kuvaratso bwino anthu wose azimayi zikomo sport kalindo paster w
@AufiThera
@AufiThera 11 дней назад
Ife wathu ndi born kalindo ✌️
@KeziaAmoss
@KeziaAmoss 11 дней назад
Kalindo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 11 дней назад
Kkkkk Koma kalindo, akuti akukondera
@NONELWANAMANYI
@NONELWANAMANYI 11 дней назад
Keep it up MR BK DC were under you Mr
@memoryyusufu
@memoryyusufu 11 дней назад
The DC mwana oooooopsa kwambiri ❤
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 11 дней назад
Dziko la Malawi lafika pothesa m, zelu ambuye bwelani
@lovemorenaluso8965
@lovemorenaluso8965 11 дней назад
😂😂😂😂the DC kusakaniza nkhanitu, mwana wooopsaa kwambiri osaopa
@SHAMILAIMEDI
@SHAMILAIMEDI 11 дней назад
More fire 🔥 big man
@user-tr4fv6ry9q
@user-tr4fv6ry9q 11 дней назад
U r indeed the pangolin.contunue fight for malawians,we are at your back
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 11 дней назад
The first here❤❤❤❤
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 11 дней назад
Koma kodi kodi chakwera ndi munthu kapena chiwanda Malawians gather here to help me...akuoneka kut satana uja Mulungu anamusiya kut malawi...apa Mulungu watiyesa mayeso ....zoona maiko onsewa ,satana akagwere kwathu kuno..Allah transfer this devil please...throw it in a country which does not prays You...as for malawians..we pray
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 11 дней назад
Tikumva kuwawa kwambiri a malawi
@dennismwenifumno994
@dennismwenifumno994 11 дней назад
Kod Border free ija inali pa manifesto ilikuti ? Malawi is about to rise.!🧑‍⚖️
@josephchipala43
@josephchipala43 11 дней назад
The legend one 💥💥 DC
@VincentChinangwa
@VincentChinangwa 11 дней назад
😂😂😂😂😂 umakwana
@PatrickViyache
@PatrickViyache 11 дней назад
Zimenezo ndipo bwana bon kalindo mukunena zoona
@user-lb5gt4uv3s
@user-lb5gt4uv3s 11 дней назад
THE Dcc much respect to you
@user-wu8kp7ui5j
@user-wu8kp7ui5j 11 дней назад
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
@successm-vt3dx
@successm-vt3dx 11 дней назад
mwana owopsa kwambiri dziko tiwotche bas kkk
@dontreybanda278
@dontreybanda278 11 дней назад
Mwana ooopya kwambiri the DC
@MphatsoMzingeni-fg2lr
@MphatsoMzingeni-fg2lr 11 дней назад
Our big man
@DYSONKUMPEREMBE
@DYSONKUMPEREMBE 11 дней назад
Machine kalindo
@crosbeygondwe5403
@crosbeygondwe5403 11 дней назад
❤❤❤❤ Bonnnnnnn Kalindoooooo
@LeonardDavid-tc5iv
@LeonardDavid-tc5iv 11 дней назад
Mulungu akudalitseni ABON anthu akufa ndi njala plz
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 11 дней назад
Zikom kwambili bon kalindo komaso ndi zoona
@user-zr5oc3rg2c
@user-zr5oc3rg2c 11 дней назад
More fire boss
@DavieWalinase
@DavieWalinase 11 дней назад
Kwatsala roadtraffic tsopano.Akupanga zopusa kwambiri
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 11 дней назад
DC mwana wohipa apule zamagona tulo
@mcdonaldkayira653
@mcdonaldkayira653 11 дней назад
Pangolin
@lameckmajiga5426
@lameckmajiga5426 11 дней назад
The D.Ciiiiiiiiiiiiii!! Ifetu tili kumbuyo kwako ndipo sitingakusiye wekhayi!! Apresident anthu achakweka pomwe zafikapa chonde mukanangosiya kupanga zomwe mukupangazo chifukwa mukukwezabe mkwiyo wa amalawi! Pamwamba pamkwiyo omwe ulipo kale! End chomwe mungaziwe palibe chanu ku 2025 ndipo mukanakhala ena mukanatula pansi udindowo before election!!
@user-cb7hp7jl7c
@user-cb7hp7jl7c 11 дней назад
I love you mr DC
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 11 дней назад
Ngati kuli munthu upusa chisilu chindere chizereza ndimunthu amene akudya zaulele koma akuzuza amamene amamudyesa chaulerezo. Nyumba galimoto petrol magesi school fees ya ana zose zaulele koma anthu amene apakupasa zimenezo mdikuwatenga ngati zisilu atsogoleri atundu anji mra mukuputa chiteze dala chizakuyabwani ndi boma lanulo
@user-qf4lq2mo6n
@user-qf4lq2mo6n 11 дней назад
More 🔥🔥🔥
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 11 дней назад
Boma la Chakwera kwake ndi kuba kupha ndi kuononga
@RashidiLastoni
@RashidiLastoni 11 дней назад
We apriceate our president more fire.
@ChristopherNikola
@ChristopherNikola 11 дней назад
Apapa zafikapa ikanangobwelapo ziwonesero ngati zaku Kenya zija
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 11 дней назад
Akuti agula mifuti 400 Monika chakwela ndiye akugawa mifuti 😂 yophela anthu oyankhula Za imfa yachilima.
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 11 дней назад
Zoona boma la cakwera ndi lokuba komanso loipitsitsa mbiri ya dziko lamalawi
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon 11 дней назад
The DC ❤❤❤❤
@LindaSonipa
@LindaSonipa 11 дней назад
🔥🔥🔥🔥
@Stevekatiwa-tp3oq
@Stevekatiwa-tp3oq 11 дней назад
Mumatiimilila BG 💪🏿💪🏿💪🏿
@IivisonMchambalinja
@IivisonMchambalinja 11 дней назад
Truth
@RiyemaDomybusiness
@RiyemaDomybusiness 11 дней назад
The diccc❤❤❤❤❤
@AstonMuneer
@AstonMuneer 11 дней назад
Kalindo always amanena zoona zokha zokha. And ife anthu sitikusintha dziko lathu chifukwa choopa boma let's do more together
@JuuuKomba
@JuuuKomba 11 дней назад
😂😂😂😂😂 mpaka pepe kaley
@JamesChiphwanya-tb3tq
@JamesChiphwanya-tb3tq 11 дней назад
NDIPO sinaone duna za bomadi zikulipira misokho olo amalowetsa zithu ulele ndipo Mr DC mau Anu ndi moto km amalawi akupusa masiku ano bwanji apa boma likuonjezatu
@ManzyLouis
@ManzyLouis 11 дней назад
Apule mutu sikugwira nanga mpaka kuphwethula ndi okaoder akhululupirila bwanji kuti katunduyo ndiwabwinobwino
@PaulBandason
@PaulBandason 4 дня назад
Mr DC tell them
@mablemathuso3903
@mablemathuso3903 10 дней назад
Kwacha yagwa kangati? Katundu tikugura pa rate yopoira ,win palibepo timapanga business kungoti nanga titani poti ntchito zikusowa.tiganizireni a business 😢chonde.
@AstonMuneer
@AstonMuneer 11 дней назад
Tiyeni tisaope aboma coz aboma akuononga mopanda chisoni
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 11 дней назад
The DC iyi nd nthaw yot ndod ituluke
@MussaHassani-zg1hm
@MussaHassani-zg1hm 11 дней назад
Thanks boss mn
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 11 дней назад
The D.C. ❤❤❤😂😂
@PetroJack
@PetroJack 11 дней назад
❤❤❤
@MosesKalenge
@MosesKalenge 11 дней назад
The DC. bon kalindo 💪💪💪💪💪💪💪💪💪♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️💥💥💥💥💥💥💥💥🫂🫂🫂🫂🫂
@VadoBukani17
@VadoBukani17 11 дней назад
Mcp woye 😂😂😂😂😂
@OweniMalokooweni-es9qx
@OweniMalokooweni-es9qx 11 дней назад
Kkkkkkkkkk😂😂😂😂😂
@IdieMatola
@IdieMatola 11 дней назад
Wathu wathu basiiii
@AgnessMzengo
@AgnessMzengo 10 дней назад
@WiskMaulana-ky6nf
@WiskMaulana-ky6nf 11 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma winiko
@FelixMunkhwayi
@FelixMunkhwayi 11 дней назад
Mumakwana aboni kalindo mupitilize zimenez amalawi tikuvutika😮
@HamidaIweni
@HamidaIweni 11 дней назад
❤❤❤❤❤😅😅😅
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 11 дней назад
Mfumu ya a mphawi
@lucksonsipolo6576
@lucksonsipolo6576 11 дней назад
😂😂😂😂😂🙌🙌
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 11 дней назад
Koma dziko ili 💔💔💔💔💔
@LeonardBanda-hg3sw
@LeonardBanda-hg3sw 11 дней назад
Tingopanga zakukenya basi asatitopese anyaniwa
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 11 дней назад
The DC sakuyamkhulapo za manganya ku mcp why
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 11 дней назад
Go konkoooooooooooooooo
Далее
BON KALINDO  LERO PA 17 JULY 2024 |
18:32
Просмотров 21 тыс.
Что с Аминой из кампуса?
00:46
Просмотров 528 тыс.
New model rc bird unboxing and testing
00:10
Просмотров 13 млн
KAMLEPO KALUA KUYANKHULA MOSANYENGELERA
29:23
Просмотров 40 тыс.
A Born Kalindo achenjeza a Pres Chakwera za Rwanda
13:47