Feeling happy when listening the voice from our beloved president, president for the poor, proud of you always, the Dddddd!!!! Cccccc!!!!!, the only true and trusted freedom fighter remaining on the ground 🔥🔥🔥🔥
A DC mwayankhula kwambiri next year tivota inu muoneka kuti umphawi wa amalawi muudziwa tangoyambitsani chipani chanu tidzakuvotereni kuti inu mzapangire amalawi munenazi I hope inuyo msidztivuta tizamva nanu kukoma
Chonde a DC athu auzeni amalawi Kuti chakwela atule Pasi udindo chifukwa akuyimbilidwa fone Kwa biligate kumuuza chakwela Kuti akwanilitse program ya catemela pakuti chakwela anatenga ndalamà zambiri Kuti amphe amalawi , ndipo chakwela akufuna kubweza ndalama Kwa biligate Koma biligate akukana akuti akufuna mbuzi zake mukhola la kumalawi tangoganizani amalawi tikuntchulidwa mbuzi Za biligate chifukwa cha chakwela,China chimene chinamumphetsa chilima ndi Ichi chilima amamuuza chakwela Kuti anthu asalandile katemela pakuti katemela uyu ndi wakupha Koma chakwela anapanga makani pakuti anali atalandila kale ndalamà Kwa biligate komaso asilikali Aku Israel anabwela Kuti azakakamize anthu kumbali ya katemela chonde amalawi tisagone Ayi
Kodi funso ndilakuti aborn kalindo basi inuyo kukhala pa air basi kungokhalira kuchauta boma basi palibe china chommwe mungapange musanene kuti onse amalawi ayi uzinena amene ukudya nawo zonazo ukuwonjeza tatopa nawe ukungofuna kusochelera amalawi ndalama umadya wekha zomwe amakupasa kuti uzipanga against ndi boma koma ma plan iweyo ulibe bwanji ubwelere kuzisuzu basi kukacha tingomva maboza akowo zaziiii tatopa nawe kape iwe ukufuna kugalukusi ntundu wamalawi munthu opanda nzeru iwe ineyo ndilibe chipani koma iweyo palibe chimene ukuthandiza amalawi koma uli porukwana ziko basi